Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2017
Galamukani! ndi magazini imene imafalitsidwa kwambiri padziko lonse.
Magazini oposa 360 miliyoni amasindikizidwa m’zilankhulo zoposa 100
ANTHU AKALE
Alhazen: Na. 6
ANTHU NDI MAYIKO
CHIPEMBEDZO
Kodi Baibulo Ndi Lochokeradi Kwa Mulungu? Na. 3
KUCHEZA NDI ANTHU
Katswiri Woona za Ubongo Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake (Rajesh Kalaria): Na. 4
Katswiri Wopanga Mapulogalamu a Pakompyuta Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake (Dr. Fan Yu): Na. 3
KUCHITA ZINTHU NDI ANTHU
Ana Akakula N’kuchoka Pakhomo (banja): Na. 4
Kodi Kuphunzitsa Ana Ntchito Zapakhomo N’kothandiza Bwanji? (kulera ana): Na. 3
Kodi Mumakonda Masewera Oika Moyo Pangozi? (achinyamata): Na. 5
Kodi Mungasonyeze Bwanji Kuti Mumayamikira Zimene Mwamuna Kapena Mkazi Wanu Amachita? (banja): Na. 1
Kumwetulira Ndi Mphatso Yofunika Kugawana: Na. 1
‘Kusankha Dzina Labwino Ndi Kwabwino Kusiyana ndi Chuma Chochuluka’: Na. 4
Mungaphunzitse Bwanji Ana Anu Kukhala Odzichepetsa? (kulera ana): Na. 6
Mungatani Ngati Muli ndi Chisoni Chifukwa cha Imfa ya Bambo Kapena Mayi Anu? (achinyamata): Na. 2
Zimene Zimachitika Ana Akakhala ndi Chisoni: Na. 2
MBONI ZA YEHOVA
“Chikondi Chimene Anatisonyeza Chinatikhudza Kwambiri”(chivomerezi ku Nepal): Na. 1
NYAMA NDI ZOMERA
Mbalame ya Kunyanja Yochititsa Chidwi Kwambiri: Na. 4
SAYANSI
Mitsempha Imene Imagwira Ntchito Ngati Ubongo: Na. 3
Njuchi Zimatera Mochititsa Chidwi: Na. 2
Nyerere Yokhala Ndi Zinthu Zoiteteza ku Dzuwa: Na. 1
Tizipatso Tokongola Kwambiri ta Buluu: Na. 4
Ubweya wa Katumbu: Na. 3
Zigoba za Nkhono Zam’madzi: Na. 5
UMOYO NDI MANKHWALA
N’chifukwa Chiyani Achinyamata Ambiri Akudwala Matenda Ovutika Maganizo? Na. 1
ZIMENE BAIBULO LIMANENA
Angelo: Na. 3
Dzina la Mulungu: Na. 6
Kuchotsa Mimba: Na. 1
Mayesero: Na. 4
Mtanda: Na. 2
Nkhondo: Na. 5
ZOCHITIKA PADZIKO
Kodi Zinthu Padzikoli Zafika Poipa Kwambiri?
Zimene Tingachite Kuti Tipulumuke Pakachitika Ngozi Zadzidzidzi: Na. 5