Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • rr tsamba 65
  • “Umete Tsitsi Lako Ndi Ndevu Zako”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Umete Tsitsi Lako Ndi Ndevu Zako”
  • Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
  • Nkhani Yofanana
  • “Mapeto Akufikira”
    Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
  • Kodi Mukudziwa?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • Mabokosi
    Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
  • Yerusalemu—“Mzinda wa Mfumu Yaikulukulu”
    Nsanja ya Olonda—1998
Onani Zambiri
Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
rr tsamba 65

BOKOSI 6A

“Umete Tsitsi Lako Ndi Ndevu Zako”

Losindikizidwa

Zimene Ezekieli anachita zinasonyeza zinthu zomwe zinali zitatsala pang’ono kuchitika mu Yerusalemu

  • Ezekieli akumeta m’mutu mwake.

    “Umete”

    Ayuda adzaukiridwa ndipo adzawonongedwa

  • Ezekieli akugwiritsa ntchito sikelo kuyezera tsitsi lake limene wameta.

    ‘Uyeze Tsitsi, Ukatero Uligawe’

    Chiweruzocho adzachita kuchikonzekera ndipo adzachipereka mwadongosolo

  • Ezekieli akuwotcha gawo lina la tsitsi limene wameta.

    ‘Uliwotche’

    Anthu ena adzafera mumzindawo

  • Ezekieli akumenya ndi lupanga gawo lina la tsitsi limene wameta.

    “Nʼkumalimenya”

    Anthu ena adzaphedwa kunja kwa mzindawo

  • Ezekieli akuuluza gawo lina la tsitsi limene wameta.

    ‘Uliuluze’

    Anthu ena adzathawa koma sadzapeza mtendere

  • Ezekieli akukulunga m’zovala zake gawo lina la tsitsi limene wameta.

    “Nʼkulikulunga”

    Anthu ena amene anali ku ukapolo adzabwerera ku Yerusalemu ndipo adzateteza kulambira koyera

Bwererani ku mutu 6, onani ndime 6-8

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena