Baibo ya Cimasulilo ca Dziko Latsopano Za m’Buku la 1 Atesalonika 1 ATESALONIKA Za m’Bukuli 1 Moni (1) Ayamika Atesalonika cifukwa ca cikhulupililo cao (2-10) 2 Utumiki wa Paulo ku Tesalonika (1-12) Atesalonika analandila mau a Mulungu (13-16) Paulo anali kulakalaka kuona Atesalonika (17-20) 3 Mwankhawa, Paulo ali ku Atene ndipo ayembekezela lipoti la ku Tesalonika (1-5) Timoteyo abweletsa lipoti lolimbikitsa (6-10) Apemphelela Atesalonika (11-13) 4 Awacenjeza kuti azipewa ciwelewele (1-8) Mupitilize kukondana kwambili (9-12) “Musamalowelele nkhani za ena” (11) Amene anafa mwa Khristu adzakhala oyambilila kuuka (13-18) 5 Kubwela kwa tsiku la Yehova (1-5) “Bata ndi mtendele!” (3) Khalani maso ndipo khalani oganiza bwino (6-11) Kuwalimbikitsa (12-24) Moni womaliza (25-28)