1
Mawu opita kwa Teofilo (1-5)
Kucitila umboni mpaka kumalekezelo a dziko lapansi (6-8)
Yesu apita kumwamba (9-11)
Ophunzila asonkhana pamodzi mogwilizana (12-14)
Matiya asankhidwa kuti alowe m’malo Yudasi (15-26)
2
Anthu alandila mzimu woyela pa Pentekosite (1-13)
Nkhani imene Petulo anakamba (14-36)
Khamu la anthu licitapo kanthu pa nkhani imene Petulo anakamba (37-41)
Akhristu acitila zinthu pamodzi (42-47)
3
4
Petulo ndi Yohane amangidwa (1-4)
Aweluzidwa pamaso pa Khoti Yaikulu ya Ayuda (5-22)
Apemphela kuti akhale olimba mtima (23-31)
Ophunzila agawana zinthu (32-37)
5
Hananiya ndi Safira (1-11)
Atumwi acita zizindikilo zambili (12-16)
Amangidwa kenako amasulidwa (17-21a)
Apelekedwanso ku Khoti Yaikulu ya Ayuda (21b-32)
Ulangizi wa Gamaliyeli (33-40)
Kulalikila kunyumba ndi nyumba (41, 42)
6
7
8
Saulo azunza ophunzila (1-3)
Utumiki wa Filipo ubala zipatso ku Samariya (4-13)
Petulo ndi Yohane atumidwa ku Samariya (14-17)
Simoni afuna kugula mzimu woyela (18-25)
Nduna ya ku Itiyopiya (26-40)
9
Saulo ali pa ulendo wopita ku Damasiko (1-9)
Hananiya atumizidwa kuti akathandize Saulo (10-19a)
Saulo alalikila za Yesu ku Damasiko (19b-25)
Saulo apita ku Yerusalemu (26-31)
Petulo acilitsa Eneya (32-35)
Dorika wowolowa manja aukitsidwa (36-43)
10
Masomphenya a Koneliyo (1-8)
Petulo aona masomphenya a nyama zoyeletsedwa (9-16)
Petulo apita kunyumba kwa Koneliyo (17-33)
Petulo alengeza uthenga wabwino kwa anthu a mitundu ina (34-43)
Anthu a mitundu ina alandila mzimu woyela ndipo abatizidwa (44-48)
11
Petulo apeleka lipoti kwa atumwi (1-18)
Baranaba ndi Saulo ku Antiokeya wa ku Siriya (19-26)
Agabo alosela za njala (27-30)
12
Yakobo aphedwa; Petulo aponyedwa m’ndende (1-5)
Petulo amasulidwa mozizwitsa (6-19)
Herode akanthidwa ndi mngelo (20-25)
13
Baranaba ndi Saulo atumizidwa ngati amishonale (1-3)
Utumiki wa ku Kupuro (4-12)
Zimene Paulo anakamba ku Antiokeya wa ku Pisidiya (13-41)
Ulosi wakuti ayambe kulalikila anthu a mitundu ina (42-52)
14
Okhulupilila awonjezeka ku Ikoniyo ndipo ayamba kutsutsidwa (1-7)
Aonedwa monga milungu ku Lusitara (8-18)
Paulo apulumuka atamuponya miyala (19, 20)
Kulimbikitsa mipingo (21-23)
Abwelela ku Antiokeya wa ku Siriya (24-28)
15
Atsutsana pa nkhani ya mdulidwe ku Antiokeya (1, 2)
Apeleka nkhaniyi ku Yerusalemu (3-5)
Akulu ndi atumwi akumana pamodzi (6-21)
Kalata yocokela ku bungwe lolamulila (22-29)
Mipingo ilimbikitsidwa ndi kalata (30-35)
Paulo ndi Baranaba apatukana (36-41)
16
Paulo asankha Timoteyo (1-5)
Munthu wa ku Makedoniya aonekela m’masomphenya (6-10)
Lidiya akhala Mkhristu ku Filipi (11-15)
Paulo ndi Sila aponyedwa m’ndende (16-24)
Woyang’anila ndende ndi a m’banja lake abatizika (25-34)
Paulo apempha akuluakulu a zamalamulo kuti apepese (35-40)
17
Paulo ndi Sila ku Tesalonika (1-9)
Paulo ndi Sila ku Bereya (10-15)
Paulo ku Atene (16-22a)
Zimene Paulo ananena ku bwalo la Areopagi (22b-34)
18
Utumiki wa Paulo ku Korinto (1-17)
Abwelela ku Antiokeya wa ku Siriya (18-22)
Paulo acoka n’kupita ku Galatiya ndi ku Filigiya (23)
Apolo wolankhula mwaluso athandizidwa (24-28)
19
Paulo ku Efeso; ena abatizika kaciwili (1-7)
Nchito yophunzitsa ya Paulo (8-10)
Apeza cipambano ngakhale kuti ena anali kukhulupilila zamizimu (11-20)
Cipolowe ku Efeso (21-41)
20
Paulo ku Makedoniya ndi ku Girisi (1-6)
Utiko aukitsidwa ku Torowa (7-12)
Acoka ku Torowa n’kupita ku Mileto (13-16)
Paulo akumana ndi akulu a ku Efeso (17-38)
21
Ulendo wa ku Yerusalemu (1-14)
Afika ku Yerusalemu (15-19)
Paulo atsatila malangizo a akulu (20-26)
Cipolowe m’kacisi; Paulo agwidwa (27-36)
Paulo aloledwa kuti alankhule ndi khamu la anthu (37-40)
22
Mawu a Paulo odziteteza pamaso pa khamu la anthu (1-21)
Paulo agwilitsa nchito unzika wake wokhala m’Roma (22-29)
Khoti Yaikulu ya Ayuda isonkhana (30)
23
Paulo alankhula pamaso pa Khoti Yaikulu ya Ayuda (1-10)
Ambuye alimbikitsa Paulo (11)
Ciwembu cofuna kupha Paulo (12-22)
Paulo atumizidwa ku Kaisareya (23-35)
24
Paulo aimbidwa milandu (1-9)
Paulo adziteteza pamaso pa Felike (10-21)
Mlandu wa Paulo uyedzekedwa kwa zaka ziwili (22-27)
25
Paulo afotokoza mlandu wake pamaso pa Fesito (1-12)
Fesito afunsila nzelu kwa Mfumu Agiripa (13-22)
Paulo aonekela pamaso pa Agiripa (23-27)
26
Paulo adziteteza pamaso pa Agiripa (1-11)
Paulo afotokoza mmene anakhalila Mkhristu (12-23)
Zimene Fesito ndi Agiripa anacita (24-32)
27
28
Gombe la ku Melita (1-6)
Atate ake Papuliyo acilitsidwa (7-10)
Ulendo wa ku Roma (11-16)
Paulo alankhula ndi Ayuda ku Roma (17-29)
Paulo alalikila molimba mtima kwa zaka ziwili (30, 31)