LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • CO-pgm18 masa. 2-3
  • Tsiku Loyamba

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tsiku Loyamba
  • Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2018
  • Nkhani Zofanana
  • Tsiku Lacitatu
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2024
  • Tsiku Laciŵili
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2018
  • Tsiku Loyamba
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2019
  • Tsiku Loyamba
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2024
Onaninso Zina
Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2018
CO-pgm18 masa. 2-3
Yoswa aŵelenga Cilamulo; Davide azungulutsa mwala na kuuponya, kumenya nawo Goliyati

Tsiku Loyamba

‘Khalani wolimba mtima kwambili’ —YOSWA 1:7

KUM’MAŴA

  • 8:20 Vidiyo ya Nyimbo

  • 8:30 Nyimbo Na. 110 na Pemphelo

  • 8:40 NKHANI YA CHEYAMANI: Yehova Ndiye Gwelo la Kulimba Mtima Kwazoona (Salimo 28:7; 31:24; 112:7, 8; 2 Timoteyo 1:7)

  • 9:10 YOSIILANA: Cimene Akhristu Oona Afunikila Kukhala Olimba Mtima

    • Polalikila (Chivumbulutso 14:6)

    • Kuti Akhalebe Oyela (1 Akorinto 16:13, 14)

    • Kuti Asamatengeko Mbali M’zandale (Chivumbulutso 13:16, 17)

  • 10:05 Nyimbo Na. 126 na Zilengezo

  • 10:15 KUŴELENGA BAIBO MWAUMOYO: “Limba Mtima, Ugwile Nchitoyi Mwamphamvu”! (1 Mbiri 28:1-20; 1 Samueli 16:1-23; 17:1-51)

  • 10:45 “Cida Ciliconse Cimene Cidzapangidwe Kuti Cikuvulaze Sicidzapambana” (Yesaya 54:17; Salimo 118:5-7)

  • 11:15 Nyimbo Na. 61 na Kupumula

Sadirake, Mesake, ndi Abedinego atuluka m’ng’anjo ya moto koma osapsa; mtumwi Paulo alemba kalata kwa Timoteyo pamene ali paukaidi wosacoka panyumba

KUMASANA

  • 12:25 Vidiyo ya Nyimbo

  • 12:35 Nyimbo Na. 69

  • 12:40 YOSIILANA: Zofooketsa, Motsutsana ndi Zothandiza Kukhala Olimba Mtima

    • Kutaya Mtima, Motsutsana ndi Ciyembekezo (Salimo 27:13, 14)

    • Kudandaula, Motsutsana ndi Kuyamikila (Salimo 27:1-3)

    • Zosangalatsa Zosayenela, Motsutsana ndi Utumiki Wakumunda (Salimo 27:4)

    • Mayanjano Oipa, Motsutsana ndi Mayanjano Abwino (Salimo 27:5; Miyambo 13:20)

    • Nzelu za Dziko, Motsutsana ndi Phunzilo Laumwini (Salimo 27:11)

    • Zikaikilo, Motsutsana ndi Cikhulupililo (Salimo 27:7-10)

  • 14:10 Nyimbo Na. 55 na Zilengezo

  • 14:20 YOSIILANA: Zimene Anaika Paciswe; Mmene Anawadalitsila

    • Hananiya, Misayeli, ndi Azariya (Danieli 1:11-13; 3:27-29)

    • Akula na Purisikila (Aroma 16:3, 4)

    • Sitefano (Machitidwe 6:11, 12)

  • 14:55 “Limbani mtima! Ndaligonjetsa Dziko Ine” (Yohane 16:33; 1 Petulo 2:21, 22)

  • 15:15 Asilikali Olimba Mtima a Khristu (2 Akorinto 10:4, 5; Aefeso 6:12-18; 2 Timoteyo 2:3, 4)

  • 15:50 Nyimbo Na. 22 na Pemphelo Lothela

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani