Tsiku Laciŵili
‘Kuonetsa kulimba mtima kowonjezeleka polankhula mawu a Mulungu mopanda mantha’ —AFILIPI 1:14
KUM’MAŴA
8:20 Vidiyo ya Nyimbo
8:30 Nyimbo Na. 76 na Pemphelo
8:40 YOSIILANA: Khalani Olimba Mtima . . .
Inu Ophunzila Baibo (Machitidwe 8:35, 36; 13:48)
Inu Acicepele (Salimo 71:5; Miyambo 2:11)
Inu Ofalitsa (1 Atesalonika 2:2)
Inu Okwatilana (Aefeso 4:26, 27)
Inu Makolo (1 Samueli 17:55)
Inu Apainiya (1 Mafumu 17:6-8, 12, 16)
Akulu mu Mpingo (Machitidwe 20:28-30)
Inu Okalamba (Danieli 6:10, 11; 12:13)
9:50 Nyimbo Na. 119 na Zilengezo
10:00 YOSIILANA: Titengele Citsanzo ca Anthu Olimba Mtima, Osati Amantha!
Osati ca Akalonga 10 aja, Koma ca Yoswa na Kalebe (Numeri 14:7-9)
Osati ca Anthu a ku Merozi, Koma ca Yaeli (Oweruza 5:23)
Osati Aneneli Onama, Koma Mikaya (1 Mafumu 22:14)
Osati ca Uliya, Koma ca Yeremiya (Yeremiya 26:21-23)
Osati ca Wolamulila Wacuma Wacinyamata, Koma ca Paulo (Maliko 10:21, 22)
10:45 UBATIZO: “Ife si Mtundu wa Anthu Obwelela M’mbuyo”! (Aheberi 10:35, 36, 39; 11:30, 32-34, 36; 1 Petulo 5:10)
11:15 Nyimbo Na. 38 na Kupumula
KUMASANA
12:35 Vidiyo ya Nyimbo
12:45 Nyimbo Na. 111
12:50 YOSIILANA: Tiphunzile Kulimba Mtima ku Zolengedwa
Mkango (Mika 5:8)
Mahosi (Yobu 39:19-25)
Mshulu [kanyama] (Salimo 91:3, 13-15)
Cozo [kambalame] (1 Petulo 3:15)
Njovu (Miyambo 17:17)
13:40 Nyimbo Na. 60 na Zilengezo
13:50 YOSIILANA: Mmene Abale Athu Amaonetsela Kulimba Mtima . . .
Mu Africa (Mateyu 10:36-39)
Ku Asia (Zekariya 2:8)
Ku Europe (Chivumbulutso 2:10)
Ku North America (Yesaya 6:8)
Ku Oceania (Salimo 94:14, 19)
Ku South America (Salimo 34:19)
15:15 Khalani Olimba Mtima Koma Osati Odzidalila (Miyambo 3:5, 6; Yesaya 25:9; Yeremiya 17:5-10; Yohane 5:19)
15:50 Nyimbo Na. 3 na Pemphelo Lothela