Zamkati
June 15, 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
YOPHUNZILA
JULY 27, 2015–AUGUST 2, 2015
Kristu Ndiye Mphamvu ya Mulungu
TSAMBA 3 • NYIMBO: 14, 109
AUGUST 3-9, 2015
TSAMBA 8 • NYIMBO: 84, 99
AUGUST 10-16, 2015
TSAMBA 13 • NYIMBO: 83, 57
AUGUST 17-23, 2015
Muzicita Zinthu Mogwilizana ndi Pemphelo Lacitsanzo—Mbali 1
TSAMBA 20 • NYIMBO: 138 Inu Ndinu Yehova (nyimbo yatsopano), 89
AUGUST 24-30, 2015
Muzicita Zinthu Mogwilizana ndi Pemphelo Lacitsanzo—Mbali 2
TSAMBA 25 • NYIMBO: 22, 68
NKHANI ZOPHUNZILA
▪ Kristu Ndiye Mphamvu ya Mulungu
▪ Anali Kukonda Anthu
Nkhanizi zikufotokoza zozizwitsa za Yesu. Zikutiphunzitsa kukhala oolowa manja ndi kukhala ndi mtima wofuna kuthandiza ena, ndiponso zikufotokoza mbali zocititsa cidwi za umunthu wake. Zikutionetsanso kuti posacedwapa tidzaona zozizwitsa zambili zikucitika padziko lonse.
▪ Tingathe Kupewa Ciwelewele
Popeza tikukhala m’dziko limene limalimbikitsa ciwelewele, zingakhale zovuta kupewa mkhalidwe woipa umenewu. Nkhaniyi itionetsa mmene ubwenzi wathu ndi Yehova, malangizo a m’Baibulo, ndi thandizo la Akristu anzathu zingatithandizile kupewa zilakolako zoipa. Ndiponso itithandiza kutsatila mfundo zapamwamba za Yehova.
▪ Muzicita Zinthu Mogwilizana ndi Pemphelo Lacitsanzo—Mbali 1
▪ Muzicita Zinthu Mogwilizana ndi Pemphelo Lacitsanzo—Mbali 2
Akristu sabweleza pemphelo lacitsanzo la Yesu, koma mapempho a m’pempheloli ali ndi tanthauzo kwa ife. Nkhani ziŵilizi zitithandiza kuona mmene tingacitile zinthu mogwilizana ndi mapempho amenewo.
NKHANI ZINA M’MAGAZINI INO
PACIKUTO: Mboni za Yehova zimagwilitsila nchito maboti kuti zikalalikile anthu amene amakhala ku zilumba za Bocas del Toro ndi Archipelago kumpoto cakumadzulo kwa dziko la Panama. Zimalalikilanso m’cinenelo ca Cingabere
KU PANAMA
KULI ANTHU
3,931,000
OFALITSA
16,217
APAINIYA
2,534
M’mipingo 309 ya ku Panama, muli apainiya apadela oposa 180. Ofalitsa pafupifupi 1,100 amatumikila m’mipingo 35 ndi m’tumagulu 15 ndipo amagwilitsila nchito cinenelo ca Cingabere. Kulinso ofalitsa pafupifupi 600 amene amatumikila m’mipingo 16 komanso tumagulu 6 ndipo amagwilitsila nchito cinenelo Camanja ca ku Panama