Ndandanda ya Mlungu wa June 17
MLUNGU WA JUNE 17
Nyimbo 48 ndi Pemphelo
□ Phunzilo la Baibo la Mpingo:
bt mutu 24 ndime 16 mpaka 21 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibo: Machitidwe 5 mpaka 7 (Mph. 10)
Na. 1: Machitidwe 5:17-32 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: Kodi Munthu Ayenela Kucita Ciani Kuti Adziŵike Kwa Yehova?—2 Tim. 2:19 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Tiyenela Kucita Ciani Kuti Tipindule ndi Nsembe ya Yesu?—rs tsa. 126 ndime 5-tsa. 127 ndime 1 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 61
Mph. 10: Kodi Tingalemekeze Bwanji Ena Muulaliki? Nkhani yocokela m’buku la Sukulu ya Utumiki, patsamba 190, ndime 1, mpaka tsamba 192, ndime 1. Mucite citsanzo cacidule coonetsa wofalitsa amene sakulemekeza mwininyumba. Ndiyeno mucitenso citsanzo cimeneco, koma panthawi ino onetsani wofalitsa akupeleka ulemu woyenela kwa mwininyumba.
Mph. 10: Thandizani Wophunzila Wanu Kukhala Wofalitsa. Nkhani yokambilana yocokela m’buku la Gulu, patsamba 78, ndime 3, mpaka pa mfundo yomaliza ili ndi kadontho kakuda patsamba 80.
Mph. 10: “Mipata Yoonjezeka Yotamanda Yehova.” Mafunso ndi mayankho. Mwacidule funsani wofalitsa mmodzi kapena aŵili amene anacita upainiya wothandiza pamene woyang’anila dela anali kucezela mpingo wanu.
Nyimbo 9 ndi Pemphelo