Ndandanda ya Mlungu wa July 22
MLUNGU WA JULY 22
Nyimbo 22 ndi Pemphelo
□ Phunzilo la Baibo la Mpingo:
bt mutu 26 ndime 9-15 ndi bokosi patsamba 208 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibo: Machitidwe 22–25 (Mph. 10)
Na. 1: Machitidwe 22:17-30 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: N’cifukwa Ciani Tinganene Kuti Sitili Mbali ya Dziko Ngakhale Kuti Timakhala M’dzikoli?—Yoh. 17:15, 16 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi N’zotheka Kuti Akristu Apite Kumwamba ndi Matupi Ao Enieni?—rs tsa. 214 ndime 4-tsa. 215 ndime 1 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 41
Mph. 10: “Mvetselani ndi Kuphunzila.” Mafunso ndi Mayankho.
Mph. 10: “Khalidwe Limene Limalemekeza Mulungu.” Mafunso ndi Mayankho. Kambilananinso “Zikumbutso za Msonkhano wa Cigawo wa 2013.”
Mph. 10: “Tengelani Citsanzo kwa Aneneli—Yoweli.” Mafunso ndi Mayankho.
Nyimbo 95 Pemphelo