Ndandanda ya Mlungu wa October 21
MLUNGU WA OCTOBER 21
Nyimbo 33 ndi Pemphelo
□ Phunzilo la Baibo la Mpingo:
jl phunzilo 14 mpaka 16 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibo: 1 Atesalonika 1 mpaka 2 Atesalonika 3 (Mph. 10)
Na. 1: 1 Atesalonika 2:9-20 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: Kodi Tingaphunzile Ciani pa Zinthu Zabwino Komanso Zoipa Zimene Solomo Anacita?—Aroma 15:4 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Baibo Imati Ciani pa Nkhani Yakuti Zipembedzo Zizicitila Zinthu Limodzi?—rs tsa. 86 ndime 1 mpaka tsa. 87 ndime 1 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 125
Mph. 15: Kodi Tiphunzilapo Ciani? Kukambilana. Ŵelengani Maliko 1:40-42, Maliko 7:32-35, ndi Luka 8:43-48 ndipo kambilanani mmene malembawa angatithandizile mu utumiki.
Mph. 15: “Njila Zocitila Kulambila kwa Pabanja.” Mafunso ndi mayankho. Pokambilana ndime 3, pemphani makolo ndi ana kuti afotokoze colinga ca kulambila kwa pabanja. Pokambilana ndime 4, pemphani omvela kuti afotokoze mmene aseŵenzetsela zinthu zosiyana-siyana kuti kulambila kwao kwa pabanja kukhale kosangalatsa kwa aliyense.
Nyimbo 88 ndi Pemphelo