Ndandanda ya Mlungu wa February 10
MLUNGU WA FEBRUARY 10
Nyimbo 57 ndi Pemphelo
□ Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
jr mutu 4 ndime 9 mpaka 14 (Mph. 30)
□ Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: Genesis 25-28 (Mph. 10)
Na. 1: Genesis 25:19-34 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: Anthu Oukitsidwa Kuti Akalamulile ndi Kristu Adzakhala Ngati Iyeyo—rs tsa. 109 ndime 4-8 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Yehova Amaiona Bwanji Nkhani Yopembedza Mafano?—bh tsa. 154-156 ndime 1-5 (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 94
Mph. 15: Kodi Tiphunzilapo Ciani? Kukambilana. Lemba la Yohane 4:6-26 liŵelengedwe. Kambilanani mmene nkhani imeneyi ingatithandizile mu ulaliki.
Mph. 15: “Kuongolela Luso Lathu mu Ulaliki—Tizilemba Tikapeza Anthu Acidwi.” Kukambilana. Pokambilana kadontho kalikonse pansi pa kamutu kakuti “Mmene Tizicitila,” pemphani omvela kuti afotokoze cifukwa cake malingalilo amenewa ndi othandiza kwambili.
Nyimbo 98 ndi Pemphelo