LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 4/14 tsa. 7
  • Ndandanda ya Mlungu wa April 28

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ndandanda ya Mlungu wa April 28
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Tumitu
  • MLUNGU WA APRIL 28
Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
km 4/14 tsa. 7

Ndandanda ya Mlungu wa April 28

MLUNGU WA APRIL 28

Nyimbo 35 ndi Pemphelo

Phunzilo la Baibulo la Mpingo:

jr mutu 7 ndime 14-20 (Mph. 30)

Sukulu ya Ulaliki:

Kuŵelenga Baibulo: Ekisodo 19-22 (Mph. 10)

Kubweleza za M’sukulu ya Ulaliki (Mph. 20)

Msonkhano wa Nchito:

Nyimbo 113

Mph. 5: Kuyambitsa Maphunzilo a Baibulo pa Ciŵelu Coyamba. Nkhani. Fotokozani zimene mpingo wakonza kaamba ka ulaliki wakumunda pa Ciŵelu coyamba m’mwezi wa May, ndipo limbikitsani onse kutengako mbali. Citani citsanzo cacidule mwa kugwilitsila nchito ulaliki wacitsanzo umene uli patsamba 8.

Mph. 15: “Tumapepala Twauthenga Twatsopano Topangidwa Mosangalatsa.” Mafunso ndi Mayankho. Citani zitsanzo ziŵili. Coyamba cionetsa wofalitsa akugaŵila tumapepala twauthenga kunyumba ndi kunyumba ndipo cina cionetse mmene wofalitsa angapitilizile makambilano paulendo wobwelelako kwa munthu amene anaonetsa cidwi.

Mph. 10: “Okonzeka Mokwanira Kukhala Aphunzitsi a Mawu a Mulungu.” Nkhani yocokela mu Nsanja ya Olonda ya February 15, 2002, masamba 24 mpaka 28. Ofalitsa ena amazengeleza kupempha anthu acidwi kuphunzila nao Baibulo cifukwa amadziona kuti ndi osayenelela kucititsa phunzilo. Komabe, Yehova ndi amene amatiyeneletsa kukhala atumiki kudzela m’Mau ake, mzimu wake woyela ndi gulu lake. Limbikitsani ofalitsa kuti azikhala ndi cidwi coyambitsa maphunzilo a Baibulo.

Nyimbo 75 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani