Ndandanda ya Mlungu wa May 26
MLUNGU WA MAY 26
Nyimbo 60 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
jr mutu 9 ndime 1 mpaka 7 (Mph. 30)
Sukulu ya ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: Ekisodo 34-37 (Mph. 10)
Na. 1: Ekisodo 34:1-16 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Na. 2: Cifukwa Cimene Malamulo Onse Amakhalidwe Abwino Sanacotsedwe Pamene Malamulo Khumi Anacotsedwa—rs tsa. 349 ndime 1-2 (Mph. 5)
Na. 3: N’cifukwa Ciani Tiyenela Kuphunzitsa Cikumbumtima Cathu?—(Iv tsa. 17-19 ndime 8 mpaka 11¶ (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 32
Mph. 10: Kuyambitsa Maphunzilo a Baibulo pa Ciŵelu Coyamba. Kukambilana. Pemphani omvela kuti afotokoze zimene anakumana nazo poyambitsa maphunzilo a Baibulo pa Ciŵelu coyamba ca mwezi. Citani citsanzo coonetsa mmene tingayambitsile phunzilo la Baibulo pa Ciŵelu coyamba mu June, pogwilitsila nchito ulaliki wacitsanzo umene uli pa tsamba 4. Limbikitsani onse kuti azitengako mbali.
Mph. 10: Kupilila Mazunzo Kumathandiza Kupeleka Umboni Wabwino (Luka 21:12, 13) Kukambilana kocokela mu Nsanja ya Olonda ya May 15, 2013 tsamba 11, ndime 12 mpaka 14. Pemphani omvela kuti afotokoze zimene aphunzilapo.
Mph. 10: Bokosi la Mafunso. Nkhani yokambidwa ndi mkulu. Pemphani acikulile kuti afotokoze mmene apindulila cifukwa cophunzitsidwa mozama coonadi ca m’Baibulo ndi makolo ao.
Nyimbo 88 ndi Pemphelo