Ndandanda ya Mlungu wa June 30
MLUNGU WA JUNE 30
Nyimbo 5 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
jr mutu 10 ndime 14 mpaka 19 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: Levitiko 14-16 (Mph. 10)
Kubweleza za M’sukulu ya Ulaliki (Mph. 20)
Msonkhano wa Nchito:
Nyimbo 58
Mph. 10: “Mufunika Kubwelelako Mwamsanga.” Nkhani. Pambuyo pake, citani citsanzo coonetsa mmene tingayambitsile maphunzilo a Baibulo mu July pa Ciŵelu coyamba pogwilitsila nchito maulaliki acitsanzo amene ali pa tsamba 8.
Mph. 20: Phunzilo Laumwini Limathandiza Kuti Tikhale Atumiki Olimba. Kukambilana kozikidwa m’buku la sukulu ya utumiki, tsamba 27-32. Funsani mafunso wofalitsa amene amadziŵika ndi zizoloŵezi zabwino za kuphunzila.
Nyimbo 69 ndi Pemphelo