Ndandanda ya Mlungu wa August 24
MLUNGU WA AUGUST 24
Nyimbo 21 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 14 ndime 10-15 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: 2 Mafumu 5-8 (Mph. 8)
Na. 1: 2 Mafumu 6:20-31 (Mph. 3 kapena zocepelapo)
Na. 2: Kodi m’Malemba Aciheberi Muli Uthenga Wotani?—igw-CIN tsa. 30 (Mph. 5)
Na. 3: Muzipewa Anthu Amene Amakonda Zoipa—w14 7/15 tsa.15 ndime 14-16 (Mph. 5)
Msonkhano wa Nchito:
Lemba la Mwezi:“Koma ine ndi a m’nyumba yanga, tizitumikila Yehova.”—Yoswa 24:15.
Nyimbo 40
Mph. 15: Zosoŵa za pampingo.
Mph. 15: Kodi Mungacite Ciani Kuti Kulambila Kwanu kwa Pabanja Kukhale Kosangalatsa? Nkhani yokambilana yocokela mu Utumiki Wathu wa Ufumu wa January 2011 tsamba 6. Ngati n’zotheka, fotokozani zinthu zina zimene mabanja angacite pa Kulambila kwa Pabanja zopezeka pa jw.org. (Pitani pa BIBLE TEACHINGS > CHILDREN.) Gogomezelani kuti kulambila kwa pabanja kuyenela kugwilizana ndi zosoŵa za banjalo. Kuyenelanso kuthandiza a m’banjalo kulimbitsa cikhulupililo cao mwa Yehova ndi malonjezo ake.
Nyimbo 130 ndi Pemphelo