Ndandanda ya Mlungu wa August 31
MLUNGU WA AUGUST 31
Nyimbo 42 ndi Pemphelo
Phunzilo la Baibulo la Mpingo:
cl mutu 14 ndime 16-20, ndi bokosi pa tsa. 147 (Mph. 30)
Sukulu ya Ulaliki:
Kuŵelenga Baibulo: 2 Mafumu 9-11 (Mph. 8)
Kubweleza za m’Sukulu ya Ulaliki (Mph. 20)
Msonkhano wa Nchito:
Lemba la Mwezi: “Koma ine ndi a m’nyumba yanga, tizitumikila Yehova.”—Yoswa 24:15.
Nyimbo 95
Mph. 10: Kugaŵila Magazini mu September. Kukambilana. Yambani ndi citsanzo coonetsa mmene tingagaŵile magazini pogwilitsila nchito maulaliki acitsanzo. Ndiyeno kambilanani maulaliki onse acitsanzo.
Mph. 10: Kodi Mumalandila “Cakudya pa Nthawi Yoyenela”? Nkhani yocokela mu Nsanja ya Mlonda ya August 15, 2014, masamba 3 mpaka 5. Limbikitsani onse kuti azigwilitsila nchito bwino cakudya ca kuuzimu cimene timalandila.
Mph. 10: Kodi Zolinga Zanu za Kuuzimu m’Caka Cautumiki ca 2016 N’zotani? Nkhani yokambilana yocokela m’buku la Gulu, tsamba 118 ndime 3. Citani citsanzo coonetsa mwamuna ndi mkazi wake akukambilana zolinga zao za kuuzimu za m’caka cautumiki catsopano.
Nyimbo 10 ndi Pemphelo