Zilengezo
◼ Zogaŵila mu August: Kabuku kakuti Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu. September ndi October: Magazini a Nsanja ya Mlonda ndi Galamukani. November: Buku lakuti, Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni kapena kamodzi mwa tumapepala twa uthenga utu: Kodi Baibo Mumaiona Bwanji?, Kodi Zinthu Zidzakhala Bwanji Mtsogolo?, Kodi Cofunika N’ciani Kuti Banja Likhale Lamtendele?, Kodi Ndani Maka-maka Amene Akulamulila Dzikoli?, Kodi Mavuto Adzathadi?, ndi Kodi N’zoona Kuti Akufa Angakhalenso ndi Moyo?
◼ Kuyambila mwezi wa September, woyang’anila dela adzayamba kukamba nkhani ya anthu onse ya mutu wakuti, “Kodi Njila za Mulungu ndi Zopindulitsadi?”