LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 February tsa. 2
  • February 1-7

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • February 1-7
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 February tsa. 2

February 1-7

NEHEMIYA 1–4

  • Nyimbo 126 ndi Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Nehemiya Anali Kukonda Kulambila Koona”: (Mph. 10)

    • [Onetsani Vidiyo Yofotokoza Buku la Nehemiya]

    • Neh. 1:11–2:3—Nehemiya anakhala ndi cimwemwe cifukwa copititsa patsogolo kulambila koona (w06 2/1 tsa. 9 ndime 7)

    • Neh. 4:14—Kuganizila kwambili za Yehova kunathandiza Nehemiya kugonjetsa amene anali kutsutsa kulambila koona (w06 2/1 tsa.10 ndime 3)

  • Kufufuza Cuma Cakuuzimu: (Mph. 8)

    • Neh. 1:1; 2:1—N’cifukwa ciani tingakambe kuti ‘caka ca 20’ cochulidwa pa Nehemiya 1:1 ndi 2:1, cikunena za nyengo imodzi? (w06 2/1 tsa 8 ndime 5)

    • Neh. 4:17, 18—Kodi munthu angagwile bwanji nchito yomanga ndi dzanja limodzi? (w06 2/1 tsa. 9 ndime 1)

    • Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kundiphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ndi mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingagwilitsile nchito mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: Neh. 3:1-14 (Mph. 4 kapena zocepelepo)

KUONJEZELA LUSO LANU MU ULALIKI

  • Konzekelani Maulaliki a Mwezi Uno (Mph. 15) Nkhani yokambilana. Pambuyo poonelela mbali iliyonse ya vidiyo ya maulaliki acitsanzo, kambilanani mfundo zofunika za mu vidiyoyo. Gogomezelani mmene wofalitsa ayalila maziko a ulendo wobwelelako. Limbikitsani omvela kulemba ulaliki wao pa danga lili patsamba loyamba.

UMOYO WATHU WACIKRISTU

  • Nyimbo 103

  • Yambani Panopa Kukonzekela kudzacitako Upainiya Wothandiza mu March kapena mu April: (Mph. 15) Nkhani yokambilana. Kambilanani mfundo zopezeka m’nkhani ya mutu wakuti “Pangani Nyengo Ino ya Cikumbutso Kukhala Yosangalatsa.” (km 2/14 2) Gogomezelani kufunika kokonzekela pasadakhale. (Miy. 21:5) Funsani mafunso ofalitsa aŵili amene anacitako upainiya wothandiza. Ndi zopinga zotani zimene anagonjetsa? Nanga ndi madalitso otani amene anapeza?

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: ia Mutu 8 ndime 1-16 (Mph. 30)

  • Kubweleza Mfundo Zimene Taphunzila ndi Kufotokoza Zomwe Tidzaphunzila Mlungu Wamaŵa (Mph. 3)

  • Nyimbo 135 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani