LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 February tsa. 1
  • Maulaliki Acitsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Maulaliki Acitsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • GALAMUKANI!
  • GALAMUKANI!
  • MVETSELANI KWA MULUNGU
  • LEMBANI ULALIKI WANU
  • Maulaliki Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Maulaliki Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 February tsa. 1
Kugaŵila kabuku ka mutu wakuti Mvetselani kwa Mulungu ku Indonesia

Alongo akugaŵila kabuku ka mutu wakuti Mvetselani kwa Mulungu ku Indonesia

Maulaliki Acitsanzo

GALAMUKANI!

Magazini ya Galamukani! Na. 1 2016 | N’zotheka Kumasangalalabe Ngakhale Muli ndi Mavuto

Funso: Ndakubweletselani magazini yatsopano ya Galamukani! Onani funso patsamba 2. Nanga inu muganiza bwanji?

Lemba: Miy. 24:10

Kugaŵila Cofalitsa: Nkhani iyi ifotokoza mfundo zina zimene zingathandize.

GALAMUKANI!

Funso: Kodi mukuvomeleza kuti n’kofunika kusankha mabwenzi abwino?

Lemba: Miy. 13:20

Kugaŵila Cofalitsa: Galamukani iyi ili ndi mfundo zimene zingatithandize kusankha mabwenzi abwino. [Musonyezeni nkhani ili pa tsa. 10-11.]

MVETSELANI KWA MULUNGU

Kabuku ka mutu wakuti Mvetselani kwa Mulungu

Funso: Kodi mungakonde kukhala m’dziko looneka conco? [Onetsani mwininyumba tsamba 2-3, ndipo yembekezani yankho.]

Lemba: Yer. 29:11

Kugaŵila Cofalitsa: Kabuku aka kaonetsa zimene tiyenela kucita kuti timvetsele kwa Mulungu n’colinga cakuti tidzakhale ndi moyo wabwino mtsogolo. [Kambilanani tsamba 4 ndi 5.]

LEMBANI ULALIKI WANU

Onani maulaliki acitsanzo amene asonyezedwa kale kuti akuthandizeni kulemba ulaliki wanu

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani