CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | NEHEMIYA 1-4
Nehemiya Anali Kukonda Kulambila Koona
Yopulinta
455 B.C.E.
Nisani (Mar./Apr.)
2:4-6 Nehemiya apempha cilolezo kuti akamangenso mpanda ku Yerusalemu, ku likulu la kulambila koona
Iyara
Sivani
Tamuzi (June/July)
2:11-15 Nehemiya wafika ndipo akuyendela mpanda
Abi (July/Aug.)
3:1; 4:7-9 Nchito yomanga iyamba ngakhale ena akutsutsa
Eloli (Aug./Sept.)
6:15 Mpanda umalizidwa pambuyo pa masiku 52
Tishiri