October 7-13
YAKOBO 3-5
Nyimbo 50 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzionetsa Nzelu Yaumulungu”: (10 min.)
Yak. 3:17—Nzelu yaumulungu ni yoyela komanso yamtendele (cl 221-222 ¶9-10)
Yak. 3:17—Nzelu yaumulungu ni yololela, yokonzeka kumvela, yodzaza ndi cifundo na zipatso zabwino (cl 223-224 ¶12; 224-225 ¶14-15)
Yak. 3:17—Nzelu yaumulungu ni yopanda tsankho, ndiponso yopanda cinyengo (cl 226-227 ¶18-19)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Yak. 4:5—Kodi pa vesi iyi, Yakobo anagwila mawu lemba liti? (w08 11/15 20 ¶6)
Yak. 4:11, 12—Kodi munthu “wonenela m’bale wake zoipa” amanenela “zoipa lamulo” m’lingalilo lotani? (w97 11/15 20-21 ¶8)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Yak. 3:1-18 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kusintha-sinthako Mawu, ndiyeno kambilanani phunzilo 10 m’bulosha ya Kuphunzitsa.
Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) w10 9/1 23-24—Mutu: N’cifukwa ciani tifunika kuulula macimo athu? Nanga tingawaulule kwa ndani? (th phunzilo 14)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (15 min.)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 86 ¶8-17
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 125 na Pemphelo