LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 October tsa. 2
  • Muzionetsa Nzelu Yaumulungu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Muzionetsa Nzelu Yaumulungu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Nkhani Zofanana
  • Nzelu Yeniyeni Imafuula
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 October tsa. 2
Mlongo akusinkha-sinkha zimene waŵelenga m’Baibo, akuganizila nthawi pamene anayambana na mlongo wina, ndipo wapita kukakhazikitsa mtendele na mlongoyo

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YAKOBO 3-5

Muzionetsa Nzelu Yaumulungu

3:17

Nzelu zocokela kwa Yehova n’zothandiza mu umoyo. Mwacitsanzo, zingatithandize kukhazikitsa mtendele na okhulupilila anzathu. Ngati munthu ali na nzelu yaumulungu, makhalidwe ake amaonetsa zimenezi.

DZIFUNSENI KUTI: ‘Pa makhalidwe a nzelu yaumulungu ali pansipa, ni ati amene naonetsako posacedwapa? Nanga ningacite ciani kuti nizionetsanso ena mwa makhalidwe amenewa?’

  • Yoyela

  • Yamtendele

  • Yololela

  • Yokonzeka kumvela

  • Yodzadza ndi cifundo na zipatso zabwino

  • Yopanda tsankho

  • Yopanda cinyengo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani