LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 November tsa. 4
  • November 11-17

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • November 11-17
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 November tsa. 4

November 11-17

2 YOHANE 1-13; 3 YOHANE 1-14-YUDA 1-25

  • Nyimbo 128 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tifunika Kumenya Nkhondo kuti Tikhalebe m’Coonadi”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la 2 Yohane.]

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la 3 Yohane.]

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Yuda.]

    • Yuda 3—‘Menyani mwamphamvu nkhondo yacikhulupililo’ (w04 9/15 11-12 ¶8-9)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Yuda 4, 12—N’cifukwa ciani anthu osaopa Mulungu amene analoŵa mu mpingo anayelekezedwa na ‘miyala ikulu-ikulu yobisika m’madzi . . . pa maphwando . . . acikondi’? (it-2 279, 816)

    • Yuda 14, 15—N’cifukwa ciani Inoki analosela za kutsogolo monga zacitika kale? Nanga ulosi wake unakwanilitsidwa bwanji? (wp17.1 12 ¶1, 3)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 2 Yoh. 1-13 (th phunzilo 12)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 1)

  • Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso, kopani cidwi cake. (th phunzilo 6)

  • Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo, ndiyeno gaŵilani kakhadi kongenela pa webusaiti yathu. (th phunzilo 11)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 87

  • Zofunikila za Mpingo: (15 min.)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu. 90

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 147 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani