January 6-12
GENESIS 1-2
Nyimbo 11 na Pemphelo
Mawu Oyamba (1 min.)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Analenga Zamoyo pa Dziko Lapansi”: (10 min.)
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Genesis.]
Gen. 1:3, 4, 6, 9, 11—Masiku a kulenga, tsiku loyamba mpaka lacitatu (it-1 527-528)
Gen. 1:14, 20, 24, 27—Masiku a kulenga, tsiku lacinayi mpaka la 6 (it-1 528 ¶5-8)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Gen. 1:1-19 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kumveketsa Phindu ya Nkhani, ndiyeno kambilanani phunzilo 13, mu bulosha ya Kuphunzitsa.
Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) w08 2/1 5—Mutu: Timakhala na Mtendele wa mu Mtima Tikadziŵa kuti Tinacita Kulengedwa (th phunzilo 11)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Kodi Mungafotokoze Cikhulupililo Canu?”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Dokota Woona za Mafupa Afotokoza Cikhulupililo Cake komanso yakuti Katswili wa za Nyama Afotokoza Cikhulupililo Cake.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 98
Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)
Nyimbo 18 na Pemphelo