May 11-17
GENESIS 38-39
Nyimbo 33 na Pemphelo
Mawu Oyamba (1 min.)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Sanamusiye Yosefe”: (10 min.)
Gen. 39:1—Yosefe anakhala kapolo ku Iguputo (w14 11/1 12 ¶4-5)
Gen. 39:12-14, 20—Yosefe ananamizilidwa na kuikidwa m’ndende (w14 11/1 14-15)
Gen. 39:21-23—Yehova anakhalabe naye Yosefe (w14 11/1 15 ¶2)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)
Gen. 38:9, 10—N’cifukwa ciani Yehova anapha Onani? (it-2 555)
Gen. 38:15-18—Kodi ni mfundo ziti zimene tiyenela kumvetsa pa zimene Yuda na Tamara anacita? (w04 1/15 30 ¶4-5)
Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mbali ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Gen. 38:1-19 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi, ndiyeno funsani omvetsela: Kodi mlongo wacita ciani kuti amveketse bwino uthenga wake kwa mwininyumba? (th phunzilo 17) Kodi wofalitsa akanafuna kugaŵilanso cofalitsa ca m’Thuboksi Yathu akanacita bwanji?
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 1)
Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso, loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 11)
Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo, ndiyeno gaŵilani kakhadi kongenela pa webusaiti yathu. (th phunzilo 6)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Khalani Monga Yosefe—Thaŵani Zaciwelewele”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Thawani Zaciwelewele.
Phunzilo la Baibo la Mpingo : (30 min.) jy mutu 114
Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)
Nyimbo 26 na Pemphelo