LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 May tsa. 4
  • Yehova Sanamusiye Yosefe

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Sanamusiye Yosefe
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Nkhani Zofanana
  • Yehova Akukuthandizani Kupambana Mayeso
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • Yehova Anapulumutsa Yosefe
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • “Kodi Mulungu Sindiye Amamasulila Maloto?”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • Yehova Amatithandiza Kupilila Mayeso
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 May tsa. 4
Yosefe ali m’ndende ku Iguputo.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 38-39

Yehova Sanamusiye Yosefe

39:1, 12-14, 20-23

Pa nthawi imene Yosefe anakumana na mayeselo ambili, Yehova anali kudalitsa “ciliconse cimene iye anali kucita.” Ndipo “anacititsa mkulu wa ndende kum’konda.” (Gen. 39:2, 3, 21-23) Kodi tiphunzilapo ciani pa nkhaniyi?

  • Mayeselo amene timakumana nawo si umboni wakuti Yehova sakondwela nafe.—Sal. 34:19

  • Tifunika kuona mmene Yehova akutidalitsila na kukhala woyamikila.—Afil. 4:6, 7

  • Tifunika kudalila Yehova kuti atithandize. —Sal. 55:22

Zithunzi: 1. M’bale ali m’jele, aŵelenga kalata yocokela ku banja lake. 2. M’bale ali pabedi m’cipatala.
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani