LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 October tsa. 2
  • October 5-11

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • October 5-11
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 October tsa. 2

October 5-11

EKSODO 31-32

  • Nyimbo 45 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Pewani Kupembedza Mafano”: (10 min.)

    • Eks. 32:1—Kukumana na mavuto si cifukwa cakuti munthu ayambe kutumikila milungu ina (w09 5/15 11 ¶11)

    • Eks. 32:4-6—Aisiraeli anasakaniza kulambila koona na kulambila konama (w12 10/15 25 ¶12)

    • Eks. 32:9, 10—Mkwiyo wa Yehova unawayakila Aisiraeli (w18.07 20 ¶14)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Eks. 31:17—Kodi Yehova anapuma pa tsiku la 7 la kulenga m’lingalilo lotani? (w19.12 3 ¶4)

    • Eks. 32:32, 33—Tidziŵa bwanji kuti ciphunzitso cakuti “munthu akangolandila Khristu ndiye kuti basi wapulumutsidwa” n’cabodza? (w87 9/1 29)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Eks. 32:15-35 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi, ndiyeno funsani mafunso aya: Kodi Brandi waseŵenzetsa bwanji mafunso mwaluso? Kodi wayala bwanji maziko a ulendo wobwelelako?

  • Ulendo Woyamba: (4 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno chulani na kukambilana vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (koma musaitambitse) (th phunzilo 9)

  • Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) w10 5/15 21—Mutu: N’cifukwa Ciani Yehova Sanam’lange Aroni Atapanga Fano la Mwana wa Ng’ombe? (th phunzilo 7)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 36

  • “Muziona Ubale Wanu na Yehova Kukhala Wamtengo Wapatali”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Tetezani Ubale Wanu na Yehova (Akol. 3:5).

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min. olo kucepelapo) jy mutu 135

  • Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)

  • Nyimbo 90 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani