LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb24 March tsa. 8
  • March 25-31

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 25-31
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
mwb24 March tsa. 8

MARCH 25-31

SALIMO 22

Nyimbo 19 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Msilikali wa Ciroma akuyang’ana covala ca Yesu pamene asilika ena aŵili akucita maele pa covalaco.

Asilikali akucita maele pa zovala za Yesu

1. Baibo Inakambilatu Zodzacitika pa Imfa ya Yesu

(Mph. 10)

Yesu adzaoneka ngati Mulungu wamusiya (Sal. 22:1; w11 8/15 15 ¶16)

Yesu adzanyozedwa (Sal. 22:7, 8; w11 8/15 15 ¶13)

Anthu adzacita maele pa zovala za Yesu (Sal. 22:18; w11 8/15 15 ¶14; onani cithunzi pacikuto)

Mlongo ali m’Paradaiso, wakhala munsi mwa mtengo pafupi na mkango wa ku mapili pamene nyama zochedwa llama zikudyela capafupi.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi Salimo 22 imalimbikitsa bwanji cikhulupililo canga kuti maulosi ena okamba za Mesiya nawonso adzakwanilitsika, monga wopezeka pa Mika 4:4?’

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 22:22—Kodi masiku ano tingatengele citsanzo ca wamasalimo m’njila ziŵili ziti? (w06 11/1 29 ¶7; w03 9/1 20 ¶1)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutigaŵilako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4.) Sal. 22:1-19 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kuyambitsa Makambilano

(Mph. 3) KUNYUMBA NA NYUMBA. (lmd phunzilo 4 mfundo 4)

5. Kubwelelako

(Mph. 4) ULALIKI WAMWAYI. Pangani ulendo wobwelelako kwa mnzanu amene anavomela kukapezekapo pa Cikumbutso. (lmd phunzilo 4 mfundo 3)

6. Nkhani

(Mph. 5) w20.07 12-13 ¶14-17—Mutu: Mmene Maulosi a m’Baibo Amalimbikitsila Cikhulupililo Cathu. (th phunzilo 20)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 95

7. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 15)

8. Phunzilo la Baibo la Mpingo

(Mph. 30) bt mutu. 7 ¶14-18, mabokosi pa mas. 57-58

Mawu Othela (3 min.) | Nyimbo 53 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani