LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb24 May tsa. 4
  • May 13-19

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • May 13-19
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
mwb24 May tsa. 4

MAY 13-19

MASALIMO 38-39

Nyimbo 125 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Musamadziimbe Mlandu Mopitilila Malile

(Mph. 10)

Kudziimba mlandu mopitilila malile kuli ngati kunyamula cikatundu colemetsa (Sal. 38:​3-8; w20.11 27 ¶12-13)

M’malo mongoganizila zolakwa zanu zakale, muziyesetsa kucita zinthu zokondweletsa Yehova (Sal. 39:​4, 5; w02-CN 11/15 20 ¶1-2)

Muzipemphela ngakhale kuti nthawi zina cingakhale covuta cifukwa codziimba mlandu (Sal. 39:12; w21.10 15 ¶4)

Zithunzi: 1. M’bale akuvutika kunyamula cikatundu colema. 2. M’bale mmodzimodzi watula cikatundu ndipo akuyembekezela mwacidwi zamtsogolo.

Ngati mumadziimba mlandu mopitilila malile, kumbukilani kuti Yehova “adzamukhululukila ndi mtima wonse” munthu wocimwa akalapa.—Yes. 55:7.

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 39:1—Ni pa nthawi iti pamene tingagwilitse nchito mfundo yakuti ‘tidzaphimba pakamwa pathu’? (w22.09 13 ¶16)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutigaŵilako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Sal. 38:​1-22 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kukhala Wosamala—Mmene Paulo Anacitila Zimenezi

(Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO, kenako kambilanani lmd phunzilo 5 mfundo 1-2.

5. Kukhala Wosamala—Tengelani Citsanzo ca Paulo

(Mph. 8) Makambilano ozikika mu lmd phunzilo 5 mfundo 3-5, komanso mbali yakuti “Onaninso Malemba Awa.”

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 44

6. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 15)

7. Phunzilo la Baibo la Mpingo

(Mph. 30) bt mutu 9 ¶17-24, bokosi pa tsa. 73

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 84 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani