JUNE 10-16
MASALIMO 48-50
Nyimbo 126 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)
1. Makolo—Thandizani Banja Lanu Kudalila Kwambili Gulu la Yehova
(Mph. 10)
Thandizani ana anu kumuyandikila Yehova na gulu lake (Sal. 48:12, 13; w22.03 22 ¶11; w11 3/15 19 ¶5-7)
Phunzitsani ana anu mbili ya gulu la Yehova (w12-CN 8/15 12 ¶5)
Mwa citsanzo canu, phunzitsani ana anu kutsatila malangizo ocokela ku gulu la Yehova (Sal. 48:14)
ZIMENE MUNGACITE PA KULAMBILA KWA PABANJA: Nthawi na nthawi muzitamba na kukambilana mavidiyo opezeka pa mbali yakuti “Gulu Lathu” pa jw.org.
2. Kufufuza Cuma Cauzimu
(Mph. 10)
Sal. 49:6, 7—Kodi Aisiraeli anayenela kukumbukila ciyani pa zinthu zabwino zimene anali nazo? (it-2-E 805)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutigaŵilako?
3. Kuŵelenga Baibo
(Mph. 4) Sal. 50:1-23 (th phunzilo 11)
4. Kucotsa Mantha—Mmene Yesu Anacitila Zimenezi
(Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO, kenako kambilanani lmd phunzilo 6 mfundo 1-2.
5. Kucotsa Mantha—Tengelani Citsanzo ca Yesu
(Mph. 8) Makambilano ozikika mu lmd phunzilo 6 mfundo 3-5, komanso mbali yakuti “Onaninso Malemba Awa.”
Nyimbo 73
6. Zofunikila za Mpingo
(Mph. 15)
7. Phunzilo la Baibo la Mpingo
(Mph. 30) bt mutu 11 ¶1-4, mawu oyamba a cigawo 4, na mabokosi pa mas. 86-87