LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb24 July tsa. 12
  • August 12-18

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 12-18
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
mwb24 July tsa. 12

AUGUST 12-18

MASALIMO 73-74

Nyimbo 36 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Kodi Tingacite Ciyani Ngati Timacitila Nsanje Anthu Omwe Salambila Mulungu?

(Mph.10)

Tingayambe kucitila nsanje anthu omwe salambila Mulungu (Sal. 73:3-5; w20.12 19 ¶14)

Tingayambe kuona zinthu moyenela ngati tilambila pamodzi na abale anzathu m’malo modzipatula (Sal. 73:17; Miy. 18:1; w20.12 19 ¶15-16)

Anthu amene salambila Mulungu ali “pamalo otelela,” koma anthu amene amalambila Mulungu amalandila “ulemelelo” (Sal. 73:18, 19, 24; w14 4/1 8 ¶5; w13-CN 2/15 25-26 ¶3-5)

Mtsikana wa Mboni akucitila kaduka anzake a m’kalasi amene akusangalala na maceza ndipo akuyang’ana pa foni.

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 74:13, 14—Kodi “Leviyatani” ayenela kuti aimila ciyani? (it-2-E 240)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Sal. 74:1-23 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kuyambitsa Makambilano

(Mph. 3) ULALIKI WAMWAYI. Pezani mpata wouzako mnzanu zimene munaphunzila pa msonkhano waposacedwa. (lmd phunzilo 2 mfundo 4)

5. Kubwelelako

(Mph. 4) ULALIKI WAPOYELA. Mupempheni kuti muziphunzila naye Baibo na kumuonetsa mmene phunzilo la Baibo limacitikila. (lmd phunzilo 8 mfundo 3)

6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupilila

(Mph. 5) Nkhani. ijwbq 89—Mutu: Kodi Zipembedzo Zonse N’zabwino? (th phunzilo 14)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 72

7. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 15)

8. Phunzilo la Baibo la Mpingo

(Mph. 30) bt mutu 14 ¶1-6, bokosi pa tsa. 112

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 98 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani