LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb24 July tsa. 13
  • August 19-25

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 19-25
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
mwb24 July tsa. 13

AUGUST 19-25

MASALIMO 75-77

Nyimbo 120 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. N’cifukwa Ciyani Simuyenela Kudzitukumula?

(Mph. 10)

Anthu odzitukumula sakondweletsa Mulungu (Sal. 75:4; 1 Tim. 3:6; w18.01 28 ¶4-5)

Udindo kapena utumiki uliwonse umene tingapatsidwe mu mpingo ni mphatso yocokela kwa Yehova ndipo sizidalila pa luso lathu (Sal. 75:​5-7; w06-CN 7/15 11 ¶3)

Anthu onyada, monga olamulila a dziko odzitukumula, Yehova adzawacititsa manyazi (Sal. 76:12)

Zithunzi: 1. M’bale akukamba nkhani pa msonkhano wa dela. 2. Pambuyo pake, m’baleyo akutamandidwa komanso kuyamikilidwa mopambanitsa, koma modzicepetsa iye akukana kutamandidwa.

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 76:10—Kodi “mkwiyo wa munthu” ungatamande bwanji Yehova? (w06-CN 7/15 11 ¶4)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Sal. 75:1–76:12 (th phunzilo 11)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kuyambitsa Makambilano

(Mph. 3) ULALIKI WAMWAYI. Tambitsani vidiyo ya pa jw.org m’cinenelo cimene munthuyo afuna. (lmd phunzilo 1 mfundo 4)

5. Kuyambitsa Makambilano

(Mph. 4) KUNYUMBA NA NYUMBA. Khalani okonzeka kusintha makambilano munthu akakuuzani kuti sakhulupilila Mulungu. (lmd phunzilo 2 mfundo 5)

6. Kupanga Ophunzila

(Mph. 5) lff phunzilo 15 mfundo 4 (lmd phunzilo 11 mfundo 3)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 127

7. Khalani Okhulupilika Mukatamandidwa

(Mph. 7) Kukambilana.

Tambitsani VIDIYO yakuti Khalani Okhulupilika Mukatamandidwa, Monga Anacitila Yesu. Kenako funsani omvela kuti:

  • Kodi mwaphunzila ciyani kwa Sergei poona mmene anacitila zinthu modzicepetsa atatamandidwa?

8. Kampeni Yapadela Yoyambitsa Maphunzilo a Baibo mu September Poseŵenzetsa Buku la Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!

(Mph. 8) Nkhani yokambidwa na woyang’anila utumiki. Limbikitsani ofalitsa kutengako mbali pa kampeniyi ndipo fotokozani makonzedwe a pa mpingo wanu.

9. Phunzilo la Baibo la Mpingo

(Mph. 30) bt mutu 14 ¶7-10, bokosi pa tsa. 110

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 95 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani