LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb24 September tsa. 12
  • October 14-20

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • October 14-20
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
mwb24 September tsa. 12

OCTOBER 14-20

MASALIMO 96-99

Nyimbo 66 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. “Muzilengeza Uthenga Wabwino”!

(Mph. 10)

Muzilalikila uthenga wabwino (Sal. 96:2; w11-CN 3/1 6 ¶1-2)

Uzani anthu uthenga wabwino wa Tsiku la Ciweluzo (Sal. 96:12, 13; w12 9/1 16 ¶1)

Auzeni colinga ca Yehova codzaza dziko lapansi na anthu amene amatamanda dzina lake (Sal. 99:1-3; w12-CN 9/15 12 ¶18-19)

M’bale wacikulile na mwamuna wina akuceza pa benchi mu paki.

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 96:1​—Kodi nthawi zambili mawu akuti “nyimbo yatsopano” akagwilitsidwa nchito amaonetsa ciyani? (it-2-E 994)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Sal. 98:1–99:9 (th phunzilo 11)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kudzipeleka​—Mmene Yesu Anacitila Zimenezi

(Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO, kenako kambilanani lmd phunzilo 10 mfundo 1-2.

5. Kudzipeleka​—Tengelani Citsanzo ca Yesu

(Mph. 8) Makambilano ozikika mu lmd phunzilo 10 mfundo 3-5, komanso mbali yakuti “Onaninso Malemba Awa.”

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 9

6. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 15)

7. Phunzilo la Baibo la Mpingo

(Mph. 30) bt mutu 16 ¶10-18

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 67 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani