LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb24 November tsa. 8
  • December 2-8

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • December 2-8
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
mwb24 November tsa. 8

DECEMBER 2-8

MASALIMO 113-118

Nyimbo 127 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Kodi Tidzamubwezela Ciyani Yehova?

(Mph. 10)

Yehova amatiteteza, amacita nafe zinthu mokoma mtima komanso amatipulumutsa (Sal. 116:​6-8; w01-CN 1/1 11 ¶13)

Tingamubwezele zabwino Yehova mwa kutsatila malamulo na mfundo zake pa umoyo wathu wonse (Sal. 116:​12, 14; w09-CN 7/15 29 ¶4-5)

Tingamubwezele zabwino Yehova mwa kupeleka ‘nsembe zomuyamikila’ (Sal. 116:17; w19.11 22-23 ¶9-11)

Mwamuna na mkazi wake akuyang’ana mtsogolo mwacidalilo. Zithunzi: Zithunzi zoonetsa njila zosiyana zimene angaseŵenzetsele nthawi yawo. 1. Akutamba pulogilamu ya pa TV yosayenela; Akuphunzila pamodzi. 2. Akugula zinthu zambilimbili; Akucita ulaliki wapoyela.

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 116:15—Kodi anthu a Mulungu “okhulupilika” ochulidwa pa vesili ndani? (w12-CN 5/15 22 ¶1-2)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Sal. 116:1–117:2 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kulimba Mtima—Mmene Yesu Anaonetsela Khalidwe Limeneli

(Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO, kenako kambilanani lmd phunzilo 12 mfundo 1-2.

5. Kulimba Mtima—Tengelani Citsanzo ca Yesu

(Mph. 8) Kukambilana. Seŵenzetsani lmd phunzilo 12 mfundo 3-5 komanso mbali yakuti “Onaninso Malemba Awa”

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 60

6. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 15)

7. Phunzilo la Baibo la Mpingo

(Mph. 30) bt mutu 19 ¶1-5, mabokosi pa mas. 149-150

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 29 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani