LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb24 November tsa. 9
  • December 9-15

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • December 9-15
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
mwb24 November tsa. 9

DECEMBER 9-15

SALIMO 119:​1-56

Nyimbo 124 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. “Kodi Wacinyamata Angakhale Bwanji Woyela pa Moyo Wake?”

(Mph. 10)

Khalani osamala nthawi zonse pa zocita zanu (Sal. 119:9; w87-CN 11/1 18 ¶10)

Muziyesetsa kutsatila zikumbutso za Mulungu (Sal. 119:​24, 31, 36; w06 6/15 25 ¶1)

Pewani kuyang’ana zinthu zopanda pake (Sal. 119:37; w10-CN 4/15 20 ¶2)

M’bale wacinyamata akucita phunzilo la munthu mwini.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ni zikumbutso ziti zimene nalandila zonithandiza kukhalabe woyela?’

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 119—Kodi salimoli linalembedwa m’njila yotani? Nanga n’cifukwa ciyani linalembedwa m’njila imeneyi? (w05-CN 4/15 10 ¶2)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Sal. 119:​1-32 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kuyambitsa Makambilano

(Mph. 3) ULALIKI WAMWAYI. Yambitsani makambilano na munthu amene mwakumana naye m’njila pocita ulaliki wa nyumba na nyumba. (lmd phunzilo 1 mfundo 4)

5. Kubwelelako

(Mph. 4) KUNYUMBA NA NYUMBA. Pa ulendo wapita, munthuyo anakuuzani kuti posacedwa anatayikilidwa wokondedwa wake mu imfa. (lmd phunzilo 9 mfundo 3)

6. Nkhani

(Mph. 5) ijwyp 83—Mutu: Kodi Ndingatani Kuti Ndisamagonje Poyesedwa? (th phunzilo 20)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 40

7. Vidiyo yakuti Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita ya December

(Mph. 10) Tambitsani VIDIYO.

8. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 5)

9. Phunzilo la Baibo la Mpingo

(Mph. 30) bt mutu 19 ¶6-13

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 21 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani