MARCH 10-16
MIYAMBO 4
Nyimbo 36 ndi Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)
Alonda akucitapo kanthu mwamsanga pamene adani akuyandikila mzinda
1. “Uteteze Mtima Wako”
(Mph. 10)
Liwu lakuti “mtima” likutanthauza umunthu wamkati (Sal. 51:6; w19.01 15 ¶4)
Tiyenela kuonetsetsa kuti tikuuteteza mtima wathu (Miy 4:23a; w19.01 17 ¶10-11; 18 ¶14; onani pacikuto)
Kuti tikhale ndi umoyo wabwino zimadalila mmene mtima wathu wophiphilitsa ulili (Miy. 4:23b; w12-CN 5/1 32 ¶2)
2. Kufufuza Cuma Cauzimu
(Mph. 10)
Miy. 4:18—Kodi vesiyi imatithandiza bwanji kumvetsa mmene Mkhristu amapitila patsogolo kuuzimu? (w21.08 8 ¶4)
Pa kuwelenga Baibulo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?
3. Kuwelenga Baibulo
(Mph. 4) Miy. 4:1-18 (th phunzilo 12)
4. Kuyambitsa Makambilano
(Mph. 3) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Munthuyo waonetsa cidwi pambuyo polandila kapepala komuitanila ku Cikumbutso. (lmd phunzilo 1 mfundo 5)
5. Kuyambitsa Makambilano
(Mph. 4) ULALIKI WAMWAYI. Itanilani ku Cikumbutso munthu amene mudziwa. (lmd phunzilo 2 mfundo 3)
6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupilila
(Mph. 5) Citsanzo. ijwfq nkhani 19—Mutu: N’cifukwa Ciyani a Mboni za Yehova Sakondwelela Isitala? (lmd phunzilo 3 mfundo 4)
Nyimbo 16
7. Vidiyo yakuti Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita ya March
(Mph. 10) Tambitsani VIDIYO.
8. Kuitanila Anthu ku Cikumbutso Kudzayamba pa Ciŵelu, March 15
(Mph. 5) Ikambidwe ndi woyang’anila utumiki. Fotokozani makonzedwe a pampingo panu okhudza kampeni, nkhani yapadela, komanso Cikumbutso. Limbikitsani ofalitsa onse kucita zambili muutumiki m’miyezi ya March ndi April.
9. Phunzilo la Baibulo la Mpingo
(Mph. 30) bt mutu 23 ¶16-19, bokosi pa tsa. 188