LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb25 March masa. 6-16
  • March 24-30

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 24-30
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2025
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2025
mwb25 March masa. 6-16

MARCH 24-30

MIYAMBO 6

Nyimbo 11 ndi Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Kodi Tingaphunzile Ciyani Kwa Nyelele?

(Mph. 10)

Tingatengepo maphunzilo ofunika kwambili tikaona mmene nyelele zimacitila zinthu (Miy. 6:6)

Ngakhale kuti zilibe wozitsogolela, mwacibadwa nyelele zimagwila nchito molimbika, zimagwilizana, ndipo zimakonzekelelatu zam’tsogolo (Miy. 6:​7, 8; it-1-E 115 ¶1-2)

Pindulani mwa kutengela mmene nyelele zimacitila zinthu (Miy. 6:​9-11; w00-CN 9/15 26 ¶3-4)

Nyelele zanyamula tuzidutswa twa mayani.

© Aerial Media Pro/Shutterstock

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Miy. 6:​16-19​—Kodi mavesiwa akupeleka mndandanda wa zinthu zonse zimene Yehova amadana nazo? (w00-CN 9/15 27 ¶3)

  • Pa kuwelenga Baibulo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?

3. Kuwelenga Baibulo

(Mph. 4) Miy. 6:​1-26 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kuyambitsa Makambilano

(Mph. 4) ULALIKI WAMWAYI. Itanilani wacibale wanu wozilala ku nkhani yapadela ndi Cikumbutso (lmd phunzilo 4 mfundo 3)

5. Kuyambitsa Makambilano

(Mph. 4) ULALIKI WAMWAYI. Pemphani abwana anu kuti akupatseni nthawi kuti mukapezekepo pa Cikumbutso. (lmd phunzilo 3 mfundo 3)

6. Kuyambitsa Makambilano

(Mph. 4) ULALIKI WAMWAYI. Itanilani munthuyo ku nkhani yapadela ndi Cikumbutso. (lmd phunzilo 5 mfundo 3)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 2

7. Cilengedwe Cimaonetsa Kuti Yehova Amafuna Kuti Tizikondwela​—Nyama Zocititsa Cidwi

(Mph. 5) Kukambilana.

Tambitsani VIDIYO. Kenako funsani omvela kuti:

  • Kodi nyama zimatiphunzitsa ciyani za Yehova?

8. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 10)

9. Phunzilo la Baibulo la Mpingo

(Mph. 30) bt mutu 24 ¶7-12, bokosi pa tsa. 193

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 126 ndi Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani