JUNE 2-8
MIYAMBO 16
Nyimbo 36 ndi Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)
1. Mafunso Atatu Amene Angatithandize Kupanga Zisankho Zabwino
(Mph. 10)
Kodi ndimadalila malangizo a Yehova? (Miy. 16:3, 20; w14 1/15 19-20 ¶11-12)
Kodi cisankho canga cidzakondweletsa Yehova? (Miy. 16:7)
Kodi ndimatengela kwambili zimene anthu ena amakamba kapena kucita? (Miy. 16:25; w13 9/15 17 ¶1-3)
DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi mafunso awa angandithandize bwanji kupanga zisankho zabwino pa nkhani ya kavalidwe ndi kudzikongoletsa?’
2. Kufufuza Cuma Cauzimu
(Mph. 10)
Miy. 16:22—Kodi “zitsilu zimalangidwa ndi kupusa kwawo komwe” m’njila yotani? (it-1-E 629)
Pa kuwelenga Baibulo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?
3. Kuwelenga Baibulo
(Mph. 4) Miy. 16:1-20 (th phunzilo 12)
4. Kuyambitsa Makambilano
(Mph. 3) ULALIKI WAMWAYI. Onetsani munthu mmene webusaiti ya jw.org ingamuthandizile. (lmd phunzilo 2 mfundo 5)
5. Kubwelelako
(Mph. 4) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Pemphani munthu amene anakanapo kuphunzila Baibulo kuti muziphunzila naye. (lmd phunzilo 9 mfundo 5)
6. Nkhani
(Mph. 5) ijwbv nkhani 40—Mutu: Kodi Miyambo 16:3 itanthauza ciyani? (th phunzilo 8)
Nyimbo 32
7. Zofunikila za Mpingo
(Mph. 15)
8. Phunzilo la Baibulo la Mpingo
(Mph. 30) bt mutu 27 ¶10-18