JUNE 23-29
MIYAMBO 19
Nyimbo 154 ndi Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)
1. Khalani Bwenzi Lenileni kwa Abale Anu
(Mph. 10)
Muzinyalanyaza zolakwa zawo (Miy. 19:11; w23.11 12-13 ¶16-17)
Muziwathandiza pa nthawi ya mavuto (Miy. 19:17; w23.07 9-10 ¶10-11)
Muziwaonetsa cikondi cosasintha (Miy. 19:22; w21.11 9 ¶6-7)
CITSANZO: Tingayelekezele zinthu zimene timakumbukila ndi zithunzi. Timasunga zithunzi zabwino zokhazokha. Mofananamo, tizikumbukila zabwino zokhazo zimene abale athu amacita.
2. Kufufuza Cuma Cauzimu
(Mph. 10)
Miy. 19:17—N’cifukwa ciyani kuthandiza anthu onyozeka kuli monga kukongoza Yehova? (w87-CN 5/15 29)
Pa kuwelenga Baibulo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?
3. Kuwelenga Baibulo
(Mph. 4) Miy. 19:1-20 (th phunzilo 2)
4. Kuyambitsa Makambilano
(Mph. 3) ULALIKI WAMWAYI. Popanda kukamba coonadi ca m’Baibulo, cezani ndi munthuyo m’njila yoti adziwe kuti ndinu wa Mboni za Yehova, ndipo m’pempheni kuti muziphunzila naye Baibulo. (lmd phunzilo 2 mfundo 4)
5. Kubwelelako
(Mph. 4) ULALIKI WAMWAYI. Pa makambilano apita, munthuyo anakuuzani kuti amakonda zacilengedwe. (lmd phunzilo 9 mfundo 4)
6. Nkhani
(Mph. 5) lmd zakumapeto A mfundo 10—Mutu: Mulungu Ali Ndi Dzina. (th phunzilo 20)
Nyimbo 40
7. Zofunikila za Mpingo
(Mph. 15)
8. Phunzilo la Baibo la Mpingo
(Mph. 30) bt mutu 28 ¶1-7