AUGUST 4-10
MIYAMBO 25
Nyimbo 154 ndi Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)
Yesu ali m’sunagoge ku Nazareti, ndipo anthu akudabwa ndi mawu ake ogwila mtima
1. Malangizo Anzelu Otithandiza Kuti Tizilankhula Bwino
(Mph. 10)
Muzisankha nthawi yabwino yolankhula (Miy. 25:11; w15-CN 12/15 19 ¶6-7)
Muzilankhula mokoma mtima komanso mwaubwenzi (Miy. 25:15; w15-CN 12/15 21 ¶15-16; onani cithunzi)
Muzilankhula mawu olimbikitsa (Miy. 25:25; w95-CN 4/1 17 ¶8)
2. Kufufuza Cuma Cauzimu
(Mph. 10)
Miy. 25:28—Kodi mwambi uwu utanthauza ciyani? (g19.3 6 ¶3)
Pa kuwelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?
3. Kuwelenga Baibo
(Mph. 4) Miy. 25:1-17 (th phunzilo 10)
4. Kuyambitsa Makambilano
(Mph. 3) ULALIKI WAMWAYI. Yambani kukambilana ndi munthu amene akuoneka wosakondwa. (lmd phunzilo 3 mfundo 3)
5. Kubwelelako
(Mph. 4) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Munthuyo wakuuzani kuti ali ndi cipembedzo cake ndipo sangasinthe. (lmd phunzilo 8 mfundo 4)
6. Nkhani
(Mph. 5) ijwyp nkhani 23—Mutu: Kodi Ndingatani Ngati Anthu Ena Amakonda Kunena za Ine? (th phunzilo 13)
Nyimbo 123
7. Zofunikila za Mpingo
(Mph. 15)
8. Phunzilo la Baibo la Mpingo
(Mph. 30) rr mutu 1 ¶15-19 ndi bokosi 1B