SEPTEMBER 8-14
MIYAMBO 30
Nyimbo 136 ndi Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)
1. “Musandipatse Umphawi Kapena Cuma”
(Mph. 10)
Timapeza cimwemwe ceniceni tikamadalila Mulungu osati cuma (Miy. 30:8, 9; w18.01 24-25 ¶10-12)
Munthu wadyela sakhutila (Miy. 30:15, 16; w87-CN 5/15 30 ¶8)
Mfundo za m’Baibo zingakuthandizeni kupewa nkhongole zosafunikila ndi nkhawa (Miy. 30:24, 25; w11-CN 6/1 10 ¶4)
ZIMENE MUNGACITE PA KULAMBILA KWA PABANJA: Monga banja, kambilanani mmene aliyense wa inu amaonela ndalama.—w24.06 13 ¶18.
2. Kufufuza Cuma Cauzimu
(Mph. 10)
Miy. 30:26—Kodi tingaphunzile ciyani kwa mbila? (w09-CN 4/15 17 ¶11-13)
Pa kuwelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?
3. Kuwelenga Baibo
(Mph. 4) Miy. 30:1-14 (th phunzilo 2)
4. Kuyambitsa Makambilano
(Mph. 4) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Gwilitsani nchito Nsanja ya Mlonda Na. 1 2025 poyambitsa makambilano. (lmd phunzilo 1 mfundo 3)
5. Kubwelelako
(Mph. 4) ULALIKI WAPOYELA. (lmd phunzilo 9 mfundo 3)
6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupilila
(Mph. 4) Nkhani. ijwbq nkhani 102—Mutu: Kodi Kuchova Njuga N’kulakwa? (th phunzilo 7)
Nyimbo 80
7. Musasoceletsedwe na Mtendele Wabodza!—Chibisa Selemani
(Mph. 5) Kukambilana.
Onetsani VIDIYO. Kenako funsani omvela kuti:
Kodi mwaphunzila ciyani kwa m’bale Selemani pa nkhani yopanga zisankho zimene zingakuthandizeni kupeza mtendele ndi cimwemwe ceniceni?
8. Vidiyo ya Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita ya September
(Mph. 10)Onetsani VIDIYO.
9. Phunzilo la Baibo la Mpingo
(Mph. 30) rr cigao 1, mutu 3 ¶1-10, vidiyo ya zimene zili m’mutu 3, ndi bokosi 3A