DECEMBER 1-7
YESAYA 3-5
Nyimbo 135 ndi Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)
1. Panali Poyenela Yehova Kuyembekezela Kuti Anthu Ake Azimumvela
(Mph. 10)
Yehova “anabzala munda wake wa mpesa” ndi kuusamalila bwino, ndipo anali kuyembekezela kuti udzabeleka zipatso zabwino (Yes. 5:1, 2, 7; ip-1-CN 73-74 ¶3-5; 76 ¶8-9)
Munda wa Yehova wa “mpesa” unangobeleka zipatso za m’chile (Yes. 5:4; w06-CN 6/15 18 ¶1)
Yehova analonjeza kuti adzausiya mundawo kuti ukhale wosalimidwa (Yes. 5:5, 6; w06-CN 6/15 18 ¶2)
DZIFUNSENI KUTI: ‘Kodi nkhani imeneyi indilimbikitsa bwanji kupewa kukhumudwitsa Yehova?’
2. Kufufuza Cuma Cauzimu
(Mph. 10)
Yes. 5:8, 9—Kodi Aisiraeli anali kucita ciyani cimene cinali kukhumudwitsa Yehova? (ip-1-CN 80 ¶18-19)
Pa kuwelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?
3. Kuwelenga Baibo
(Mph. 4) Yes. 5:1-12 (th phunzilo 5)
4. Kuyambitsa Makambilano
(Mph. 3) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Sewenzetsani vidiyo ya mu Thuboksi ya Zida Zophunzitsila. (lmd phunzilo 1 mfundo 5)
5. Kubwelelako
(Mph. 4) ULALIKI WAMWAYI. Uzani munthuyo za JW Laibulale, ndipo m’thandizeni kuicita daunilodi pafoni yake. (lmd phunzilo 9 mfundo 5)
6. Kupanga Ophunzila
(Mph. 5) Limbikitsani wophunzila Baibo amene akutsutsidwa ndi a m’banja lake. (lmd phunzilo 12 mfundo 4)
Nyimbo 65
7. Zofunikila za Mpingo
(Mph. 15)
8. Phunzilo la Baibo la Mpingo
(Mph. 30) rr mutu 7 ¶8-15 ndi bokosi 7A