1
2
Okhulupilila nyenyezi apita kukaona Yesu (1-12)
Athaŵila ku Iguputo (13-15)
Herode akupha ana aamuna (16-18)
Abwelela ku Nazareti (19-23)
3
4
Mdyelekezi ayesa Yesu (1-11)
Yesu ayamba kulalikila ku Galileya (12-17)
Yesu aitana ophunzila ake oyamba (18-22)
Yesu alalikila, kuphunzitsa, na kucilitsa (23-25)
5
6
7
8
Wakhate acilitsidwa (1-4)
Cikhulupililo ca kapitawo wa asilikali (5-13)
Yesu acilitsa anthu ambili ku Kaperenao (14-17)
Mmene tingatsatilile Yesu (18-22)
Yesu aleketsa cimphepo ca mkuntho pa nyanja (23-27)
Yesu atumiza ziŵanda m’nkhumba (28-34)
9
Yesu acilitsa munthu wakufa ziwalo (1-8)
Yesu aitana Mateyo (9-13)
Funso pa nkhani ya kusala kudya (14-17)
Mwana wamkazi wa Yairo; mayi agwila covala cakunja ca Yesu (18-26)
Yesu acilitsa anthu akhungu na munthu wosalankhula (27-34)
Zokolola n’zambili koma anchito ni ocepa (35-38)
10
Atumwi 12 (1-4)
Malangizo a ulaliki (5-15)
Ophunzila a Yesu adzazunzidwa (16-25)
Opani Mulungu osati anthu (26-31)
Lupanga osati mtendele (32-39)
Kulandila ophunzila a Yesu (40-42)
11
Yohane M’batizi atamandidwa (1-15)
Yesu adzudzula m’badwo wopanda cikhulupililo (16-24)
Yesu atamanda Atate wake cifukwa cokonda anthu odzicepetsa (25-27)
Joko ya Yesu ni yotsitsimula (28-30)
12
Yesu ndiye “Mbuye wa Sabata” (1-8)
Munthu wa dzanja lopuwala acilitsidwa (9-14)
Mtumiki wa Mulungu wokondedwa (15-21)
Yesu atulutsa ziŵanda mwa mphamvu ya mzimu woyela (22-30)
Chimo limene silingakhululukidwe (31, 32)
Mtengo umadziŵika na zipatsa zake (33-37)
Cizindikilo ca Yona (38-42)
Mzimu wonyansa ukabwelela mwa munthu (43-45)
Amayi a Yesu na abale ake (46-50)
13
14
Yohane M’batizi adulidwa mutu (1-12)
Yesu adyetsa anthu 5,000 (13-21)
Yesu ayenda pamadzi (22-33)
Yesu acilitsa anthu ku Genesareti (34-36)
15
Kuvumbula miyambo ya anthu (1-9)
Zodetsa munthu zimacokela mu mtima (10-20)
Cikhulupililo cacikulu ca mayi wa ku Foinike (21-28)
Yesu acilitsa matenda osiyana-siyana (29-31)
Yesu adyetsa anthu 4,000 (32-39)
16
Apempha cizindikilo (1-4)
Zofufumitsa za Afarisi na Asaduki (5-12)
Makiyi a Ufumu (13-20)
Yesu anenelatu za imfa yake (21-23)
Zimene ophunzila oona a Yesu amacita (24-28)
17
Kusandulika kwa Yesu (1-13)
Cikhulupililo cocepa ngati kanjele ka mpilu (14-21)
Kaciŵili, Yesu anenelatu za imfa yake (22, 23)
Akhoma msonkho na khobili lotengedwa m’kamwa mwa nsomba (24-27)
18
Wamkulu kwambili mu Ufumu wa kumwamba (1-6)
Zopunthwitsa (7-11)
Fanizo la nkhosa yosocela (12-14)
Mmene tingabwezele m’bale wathu (15-20)
Fanizo la kapolo wosakhululukila mnzake (21-35)
19
Ukwati na cisudzulo (1-9)
Mphatso ya umbeta (10-12)
Yesu adalitsa ana (13-15)
Funso la mnyamata wacuma (16-24)
Kudzimana cifukwa ca Ufumu (25-30)
20
Ogwila nchito m’munda wa mpesa komanso malipilo awo ofanana (1-16)
Yesu akambilatunso za imfa yake (17-19)
Apempha malo apamwamba mu Ufumu (20-28)
Yesu acilitsa anthu aŵili akhungu (29-34)
21
Yesu atamandidwa poloŵa mu Yerusalemu (1-11)
Yesu ayeletsa kacisi (12-17)
Atembelela mtengo wa mkuyu (18-22)
Anthu akayikila mphamvu za Yesu (23-27)
Fanizo la ana aŵili (28-32)
Fanizo la alimi akupha (33-46)
22
Fanizo la phwando la ukwati (1-14)
Mulungu na Kaisara (15-22)
Funso pa nkhani ya kuuka kwa akufa (23-33)
Malamulo aŵili aakulu kwambili (34-40)
Kodi Khristu ni mwana wa Davide? (41-46)
23
Musamatengele alembi na Afarisi (1-12)
Tsoka kwa alembi na Afarisi (13-36)
Yesu alilila Yerusalemu (37-39)
24
25
26
Ansembe akonza ciwembu cakuti aphe Yesu (1-5)
Yesu athilidwa mafuta onunkhila (6-13)
Pasika wothela komanso kupelekedwa kwa Yesu (14-25)
Kukhazikitsidwa kwa Mgonelo wa Ambuye (26-30)
Yesu akambilatu kuti Petulo adzamukana (31-35)
Yesu apemphela m’munda wa Getsemane (36-46)
Yesu agwidwa (47-56)
Yesu azengedwa mlandu m’Khoti Yaikulu ya Ayuda (57-68)
Petulo akana Yesu (69-75)
27
Yesu apelekedwa kwa Pilato (1, 2)
Yudasi adzimangilila (3-10)
Yesu aonekela pamaso pa Pilato (11-26)
Yesu acitidwa zacipongwe (27-31)
Amukhomelela pa mtengo ku Gologota (32-44)
Imfa ya Yesu (45-56)
Yesu aikidwa m’manda (57-61)
Akhwimitsa citetezo pa manda a Yesu (62-66)
28