1
Ulaliki wa Yohane M’batizi (1-8)
Ubatizo wa Yesu (9-11)
Yesu ayesedwa na Satana (12, 13)
Yesu ayamba kulalikila ku Galileya (14, 15)
Yesu aitana ophunzila ake oyamba (16-20)
Yesu atulutsa mzimu wonyansa (21-28)
Yesu acilitsa anthu ambili ku Kaperenao (29-34)
Apemphela kwayekha (35-39)
Wakhate acilitsidwa (40-45)
2
Yesu acilitsa munthu wakufa ziwalo (1-12)
Yesu aitana Levi (13-17)
Funso pa nkhani ya kusala kudya (18-22)
Yesu, ‘Mbuye wa Sabata’ (23-28)
3
Munthu wa dzanja lopuwala acilitsidwa (1-6)
Khamu lalikulu la anthu m’mbali mwa nyanja (7-12)
Atumwi 12 (13-19)
Kunyoza mzimu woyela (20-30)
Mayi a Yesu na abale ake (31-35)
4
5
6
Yesu akanidwa mu mzinda wa kwawo (1-6)
Atumwi 12 apatsidwa malangizo a ulaliki (7-13)
Imfa ya Yohane M’batizi (14-29)
Yesu adyetsa anthu 5,000 (30-44)
Yesu ayenda pa madzi (45-52)
Acilitsa anthu ku Genesareti (53-56)
7
Kuvumbula miyambo ya anthu (1-13)
Zodetsa munthu zimacokela mu mtima (14-23)
Cikhulupililo ca mayi wacisirofoinike (24-30)
Munthu wogontha acilitsidwa (31-37)
8
Yesu adyetsa anthu 4,000 (1-9)
Apempha cizindikilo (10-13)
Zofufumitsa za Afarisi na za Herode (14-21)
Munthu wakhungu acilitsidwa ku Betsaida (22-26)
Petulo azindikila Khristu (27-30)
Yesu anenelatu za imfa yake (31-33)
Zimene ophunzila oona a Yesu amacita (34-38)
9
Kusandulika kwa Yesu (1-13)
Kamnyamata kogwidwa na ciŵanda kacilitsidwa (14-29)
Yesu akambilatunso za imfa yake (30-32)
Ophunzila akangana zakuti wamkulu ndani (33-37)
Aliyense amene satsutsana nafe ali ku mbali yathu (38-41)
Zopunthwitsa (42-48)
“Khalani na mcele mwa inu” (49, 50)
10
Ukwati na cisudzulo (1-12)
Yesu adalitsa ana (13-16)
Funso la munthu wacuma (17-25)
Kudzimana cifukwa ca Ufumu (26-31)
Yesu akambilatunso za imfa yake (32-34)
Pempho la Yakobo na Yohane (35-45)
Batimeyu wakhungu acilitsidwa (46-52)
11
Yesu atamandidwa poloŵa mu Yerusalemu (1-11)
Atembelela mtengo wa mkuyu (12-14)
Yesu ayeletsa kacisi (15-18)
Phunzilo pa mtengo wa mkuyu wofota (19-26)
Ulamulilo wa Yesu utsutsidwa (27-33)
12
Fanizo la alimi akupha (1-12)
Mulungu na Kaisara (13-17)
Funso pa nkhani ya kuuka kwa akufa (18-27)
Malamulo aŵili aakulu kwambili (28-34)
Kodi Khristu ni mwana wa Davide? (35-37a)
Yesu acenjeza anthu za alembi (37b-40)
Tumakobili tuŵili twa mkazi wamasiye wosauka (41-44)
13
14
Ansembe akonza ciwembu cakuti aphe Yesu (1, 2)
Yesu athilidwa mafuta onunkhila (3-9)
Yudasi apeleka Yesu (10, 11)
Pasika wothela (12-21)
Kukhazikitsa Mwambo wa Mgonelo wa Ambuye (22-26)
Yesu akambilatu kuti Petulo adzamukana (27-31)
Yesu apemphela pa malo ochedwa Getsemani (32-42)
Yesu agwidwa (43-52)
Yesu azengedwa mlandu m’Khoti Yaikulu ya Ayuda (53-65)
Petulo akana Yesu (66-72)
15
Yesu aonekela pamaso pa Pilato (1-15)
Yesu acitidwa zacipongwe pamaso pa anthu (16-20)
Amukhomelela pa mtengo ku Gologota (21-32)
Imfa ya Yesu (33-41)
Yesu aikidwa m’manda (42-47)
16