1
Mawu oyamba (1-7)
Paulo alakalaka kupita ku Roma (8-15)
Wolungama adzakhala ndi moyo cifukwa ca cikhulupililo (16, 17)
Anthu osalambila Mulungu alibe cifukwa comveka cosakhulupilila kuti Mulungu aliko (18-32)
2
Ciweluzo ca Mulungu kwa Ayuda ndi Agiriki (1-16)
Ayuda komanso Cilamulo (17-24)
Mdulidwe wa mumtima (25-29)
3
“Mulungu angapezekebe kuti akukamba zoona” (1-8)
Ayuda ndi Agiriki, onse amalamulilidwa ndi ucimo (9-20)
Kukhala wolungama cifukwa ca cikhulupililo (21-31)
4
5
Kuyanjanitsidwanso ndi Mulungu kudzela mwa Khristu (1-11)
Imfa kudzela mwa Adamu, moyo kudzela mwa Khristu (12-21)
6
Moyo watsopano kudzela mu ubatizo wogwilizana ndi Khristu (1-11)
Musalole kuti ucimo upitilize kulamulila m’matupi anu (12-14)
Kucoka ku ukapolo wa ucimo n’kukhala akapolo a Mulungu (15-23)
7
Fanizo la mmene munthu amamasukila ku Cilamulo (1-6)
Ucimo udziwika cifukwa ca Cilamulo (7-12)
Kulimbana ndi ucimo (13-25)
8
Mzimu umabweletsa moyo ndi ufulu (1-11)
Mzimu umacitila umboni (12-17)
Cilengedwe cikuyembekezela ufulu wa ana a Mulungu (18-25)
“Mzimu umacondelela m’malo mwathu” (26, 27)
Kusankhidwilatu ndi Mulungu (28-30)
Tikugonjetsa zinthu zonsezi cifukwa ca cikondi ca Mulungu (31-39)
9
Paulo amvela cisoni Isiraeli wakuthupi (1-5)
Mbadwa zenizeni za Abulahamu (6-13)
Sitingatsutse zimene Mulungu wasankha (14-26)
Ocepa cabe ndi amene adzapulumuke (27-29)
Aisiraeli anapunthwa (30-33)
10
11
Si Aisiraeli onse amene anakanidwa (1-16)
Fanizo la mtengo wa maolivi (17-32)
Kuzama kwa nzelu za Mulungu (33-36)
12
Mupeleke matupi anu monga nsembe yamoyo (1, 2)
Mphatso zosiyanasiyana koma thupi limodzi (3-8)
Malangizo pa umoyo wathu wacikhristu (9-21)
13
Kugonjela olamulila (1-7)
Cikondi cimakwanilitsa Cilamulo (8-10)
Kuyenda monga anthu ocita zinthu masana (11-14)
14
15
Landilanani ngati mmene Khristu anakulandililani (1-13)
Paulo, mtumiki kwa anthu a mitundu ina (14-21)
Mmene Paulo anakonzela ulendo wake (22-33)
16
Paulo adziwitsa mpingo za mlongo Febe (1, 2)
Moni kwa Akhristu a ku Roma (3-16)
Awacenjeza za anthu obweletsa magawano (17-20)
Moni wocokela kwa anchito anzake a Paulo (21-24)
Cinsinsi copatulika ciululika (25-27)