Phunzilani Zambili Pa Jw.Org
Ni nkhani iti imene mungakonde kuiŵelenga?
Zimene mungacite kuti zinthu ziziyenda bwino m’cikwati canu
Onani nkhani ya ku Chichewa yakuti “Kodi Mungatani Kuti Zipangizo Zamakono Zisamakusokonezeni?”
Mmene mungaphunzitsile ana anu makhalidwe abwino
Onani vidiyo ya zithunzi zojambula pamanja yakuti “Kodi Zipangizo Zanu Zimakulamulilani?”
Baibo ingakuthandizeni inu na banja lanu kukhala na umoyo wacimwemwe palipano komanso ciyembekezo ca tsogolo labwino.
PA JW.ORG PALINSO: Maphunzilo a Baibo a pa Intaneti. Ni aulele, ndipo simuyenela kucita kulembetsa.