Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambili Onena za Umoyo?
Kodi mayankho angapezeke mu . . .
sayansi?
nzelu za anthu?
Baibulo?
WOLEMBA BAIBULO ANATI KWA MULUNGU
“Ndithandizeni kukhala wozindikila . . . Mau anu onse ndi coonadi.”—Salimo 119:144, 160, Baibulo la Dziko Latsopano.
Baibulo likuyankha anthu mamiliyoni.
Kodi inunso mungakhale mmodzi wa anthu amenewa?
Webu saiti ya jw.org ingakuthandizeni.
ŴELENGANI zopezeka pa Webu saiti
Baibulo m’zinenelo zoposa 100
Mayankho a mafunso a m’Baibulo
Thandizo la mabanja
ONELELANI mavidiyo onena za m’Baibulo
Maphunzilo ndi nyimbo za ana
Malangizo a acinyamata
Zinthu zoonetsa cikhulupililo
TENGANI zopezeka pa Webu saiti
Bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!
Magazini ya Nsanja ya Mlonda ndi Galamukani!
KODI NDI FUNSO LITI LIMENE LIMAKUVUTITSANI MAGANIZO KWAMBILI?
Kodi colinga ca moyo n’ciani?
Kodi tiyenela kuimba mlandu Mulungu cifukwa ca mavuto athu?
Cimacitika n’ciani mukamwalila?
Pezani mayankho a m’Baibulo a mafunso amenewa pa jw.org.
(Pitani pa BIBLE TEACHINGS > BIBLE QUESTIONS ANSWERED)