Tsiku Laciŵili
“Kondwelani ndi ciyembekezoco. Pililani cisautso” —AROMA 12:12
KUM’MAŴA
8:20 Nyimbo za Pavidiyo
8:30 Nyimbo 68 na Pemphelo
8:40 YOSIILANA: Mmene Yehova ‘Amapatsila Mphamvu Zopilila na Kutonthoza’ . . .
Ofooka ndi Ovutika Maganizo (Aroma 15:4, 5; 1 Atesalonika 5:14; 1 Petulo 5:7-10)
Ofunikila Thandizo la Kuthupi (1 Timoteyo 6:18)
“Onyozeka ndi Ana Amasiye” (Salimo 82:3)
Okalamba (Levitiko 19:32)
9:50 Nyimbo 90 na Zilengezo
10:00 YOSIILANA: Mangani Nyumba Imene Idzakhalitsa
‘Khutilani ndi Zimene Muli Nazo pa Nthawiyo’ (Aheberi 13:5; Salimo 127:1, 2)
Tetezani Ana Anu ku “Zinthu Zoipa” (Aroma 16:19; Salimo 127:3)
Phunzitsani Ana Anu ‘m’Njila Yowayenelela’ (Miyambo 22:3, 6; Salimo 127:4, 5)
10:45 NKHANI YA UBATIZO: ‘Musaope Cocititsa Mantha Ciliconse’! (1 Petulo 3:6, 12, 14)
11:15 Nyimbo 139 na Kupumula
KUMASANA
12:35 Nyimbo za Pavidiyo
12:45 Nyimbo 43
12:50 YOSIILANA: Tengelani Citsanzo ca “Anthu Amene Anapilila”
Yosefe (Genesis 37:23-28; 39:17-20; Yakobo 5:11)
Yobu (Yobu 10:12; 30:9, 10)
Mwana Wamkazi wa Yefita (Oweruza 11:36-40)
Yeremiya (Yeremiya 1:8, 9)
13:35 SEŴELO: “Kumbukilani Mkazi wa Loti”—Mbali 2 (Luka 17:28-33)
14:05 Nyimbo 75 na Zilengezo
14:15 YOSIILANA: Zolengedwa Zimatiphunzitsa Kupilila
Ngamila (Yuda 20)
Mtengo wa Paini (Akolose 2:6, 7; 1 Petulo 5:9, 10)
Gulugufe (2 Akorinto 4:16)
Mbalame Yochedwa Arctic Tern (1 Akorinto 13:7)
Mbalame Yochedwa Plova (Aheberi 10:39)
Mtengo wa Akesha (Aefeso 6:13)
15:15 Acicepele—Yehova Amakondwela Mukamapilila! (Miyambo 27:11)
15:50 Nyimbo 89 na Pemphelo Lothela