Tsiku Lacitatu
“Amene adzapilile mpaka pa mapeto, ndiye amene adzapulumuke”—MATEYU 24:13
KUM’MAŴA
8:20 Nyimbo za Pavidiyo
8:30 Nyimbo 83 na Pemphelo
8:40 YOSIILANA: Tifunika ‘Kuthamanga Mopilila’
Thamangani Kuti Mupambane! (1 Akorinto 9:24)
Konzekelani Mwakhama (1 Akorinto 9:25-27)
Tayani Zolemetsa Zosafunika (Aheberi 12:1)
Tengelani Zitsanzo Zabwino (Aheberi 12:2, 3)
Idyani Zakudya Zopatsa Thanzi (Aheberi 5:12-14)
Imwani Madzi Ambili (Chivumbulutso 22:17)
Tsatilani Malamulo a Mpikisano (2 Timoteyo 2:5)
Khalani na Cidalilo Cakuti Mudzalandila Mphoto (Aroma 15:13)
10:10 Nyimbo 130 na Zilengezo
10:20 NKHANI YA ANTHU ONSE: Musataye Mtima! (Yesaya 48:17; Yeremiya 29:11)
10:50 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
11:20 Nyimbo 148 na Kupumula
KUMASANA
12:35 Nyimbo za Pavidiyo
12:45 Nyimbo 142
12:50 SEŴELO: “Kumbukilani Mkazi wa Loti”—Mbali 3(Luka 17:28-33)
13:20 Nyimbo 65 na Zilengezo
13:30 “Uziwayembekezelabe . . . Iwo Sadzacedwa!”(Habakuku 2:3)
14:30 Nyimbo 154 na Pemphelo Lothela