Tsiku Lacitatu
“Mulungu amene amapeleka ciyembekezo akudzazeni ndi cimwemwe conse”—Aroma 15:13
M’maŵa
8:20 Vidiyo ya Nyimbo
8:30 Nyimbo Na. 101 na Pemphelo
8:40 YOSIYILANA: Anafesa Mtendele na Kututanso Mtendele
• Yosefe na Abale Ake (Agalatiya 6:7, 8; Aefeso 4:32)
• Agibeoni (Aefeso 5:17)
• Gidiyoni (Oweruza 8:2, 3)
• Abigayeli (1 Samueli 25:27-31)
• Mefiboseti (2 Samueli 19:25-28)
• Paulo na Baranaba (Machitidwe 15:36-39)
• Zitsanzo Zamakono (1 Petulo 2:17)
10:05 Nyimbo Na. 28 na Zilengezo
10:15 NKHANI YA ANTHU ONSE: N’zotheka Kukhala Paubwenzi na Mulungu—Motani? (Yakobo 4:8; 1 Yohane 4:10)
10:45 Nyimbo Na. 147 na Kupumula
Masana
12:35 Vidiyo ya Nyimbo
12:45 Nyimbo Na. 23
12:50 SEŴELO LA M’BAIBO: Yehova Akutitsogolela Panjila ya Mtendele—Gawo 2 (Yesaya 48:17, 18)
13:30 Nyimbo Na. 139 na Zilengezo
13:40 Mtendele wa Cilengedwe Conse Udzabwela Ndithu! (Aroma 16:20; 1 Akorinto 15:24-28; 1 Yohane 3:8)
14:40 Nyimbo Yatsopano na Pemphelo Lothela